Breaking: DPP treasurer arrested: Caught bonking another man’s wife

Advertisement
Happy Kumwenda
Happy Kumwenda
Kumwenda was previously shot

Malawi ruling Democratic Progressive Party (DPP) treasurer for the Northern Region, Happy Kumwenda, is in police custody.

Reports monitored by this publication indicate that Kumwenda was caught in the act having failed to tame his manhood.

The treasurer, who was previously shot, is well known in Mzuzu for opening his zip carelessly.

More details to follow, please visit this page again shortly.

Advertisement

290 Comments

 1. ine ndimaona ngati mutiuzA kuti Chipani Cha DPP achipezelera chilkupanga chigololo….Hahahaha…I am telling you DpP simudzaitha guyz…we are driving this country until chakumtima chathu chidzatichoke…..DpP woyeeeeeee!!!!!!!!!!……..

 2. Kungoti zamuseli zimakoma zilingati black market, koma mdalayu waonjenza pakana magalasi kuchibwenzi nkana amugwira samaona patali nanga mkazi alikuti

 3. Kodi munthuyi amanyengera DPP? Mwayamba ndale eti sizikuthandizanitu ngati akutumani nyasi za atola mkani ngati inu sitikuzifuna shupt

 4. MALAWI 24,Atola khani ake ovetsa chisoni Nakha khani iyi ikugwilizana ndi DPP? Banjalo LiLindi akhoswe ngomwe akaweluze, Mamuna amafusila kumene m’kaziyo anali ndiwufulu wokwana, ndikati ndiwonetsetse bajamo muli mavuto ,komaso khaniyi sikugwilizana ndi ntchito yamuthu or DPP ,Osayikapo dzina lake bwanji fack u mw24 news

 5. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..

 6. Is the woman in police custody aswell? Coz mkulu wangayu sampanga yekha… Nayeso mkaziyu anaiyanika 4 another woman’s man

 7. whats wrong when someone bonks with another mans wife maybe its the woman who was the masterminder of the deal. stop talking that useless thing talk about malawi’s economy and the stupidity of mr peter ibu mutharika for guarding homosexuals.

 8. whats wrong when someone bonks with another mans wife maybe its the woman who was the masterminder of the deal. stop talking that useless thing talk about malawi’s economy and the stupidity of mr peter ibu mutharika for guarding homosexuals.

 9. mwaona okhao Basi? enawa bwanji? zomwe mumapanga a Malawi 24 ndimadabwa nanu.Kodi mbs sangatseke company imeneyi? bolanso yachibagi ija inali bwino koma izi zaziiii

 10. mwaona okhao Basi? enawa bwanji? zomwe mumapanga a Malawi 24 ndimadabwa nanu.Kodi mbs sangatseke company imeneyi? bolanso yachibagi ija inali bwino koma izi zaziiii

 11. Mbamva Izi Ndizimene Zikutibela Ndalama Zathu Zamitsokho Yathu,panyapanu Nonse Adpp Komaso Aja Amavala Zisoti Zabeni Chifukwa Amakonda Dpp.

 12. aaaaaaa at pot nd wa DPP mwina mkukhululuka! njeeee malamulo agwire ntchito apa! athothe munthuyo mwina nchitidwe umenewu mkuchepako

 13. He should be locked he is going out with someone’s wife like mbeta zikusowa mabanja ku Malawiko zatha.He is an idiot let him face the consequences of justice.Anthu achitidwe otelewu akuchulukila akalowe ena atengele phunziro DPP yapeza malamulo adakalipo ndikanakhala mgulu lomugwira choyamba akanalandira zikoti 100 kaye

 14. Way to go man…. Well the world now knows that your dick aint just for peeing but also for screwing other peoples spouses…lol

 15. Way to go man…. Well the world now knows that your dick aint just for peeing but also for screwing other peoples spouses…lol

 16. Lamulo siliona nkhope. Ngati lilipo lamulo limene aphwanya pa zomwe achita ndie chilungamo chiyendepo. A Kumwenda chalongola kuti mukamba kale chomene uchitilo winu uwu. Banakazi bambula banalume bali mbwelelele mukubaleka. Apa mwajinangiska mbiri yinu, kugomezgeka kwinu ndiposo nakuzirwa kwinu kwamala. Better hule likupanga vinthu pakweru. Ine nayowoyapo waka kweni bamupachaninge mbavya malango. Naszondera pa RUMPHI

 17. Lamulo siliona nkhope. Ngati lilipo lamulo limene aphwanya pa zomwe achita ndie chilungamo chiyendepo. A Kumwenda chalongola kuti mukamba kale chomene uchitilo winu uwu. Banakazi bambula banalume bali mbwelelele mukubaleka. Apa mwajinangiska mbiri yinu, kugomezgeka kwinu ndiposo nakuzirwa kwinu kwamala. Better hule likupanga vinthu pakweru. Ine nayowoyapo waka kweni bamupachaninge mbavya malango. Naszondera pa RUMPHI

 18. Akuluwa amamwa mwamuna sakalamba nkhondo ku bed; kudziletsa kumavuta zikatero chifukwa cholembera chimayamba kututuma mosalekeza. kkkk!

 19. Akuluwa amamwa mwamuna sakalamba nkhondo ku bed; kudziletsa kumavuta zikatero chifukwa cholembera chimayamba kututuma mosalekeza. kkkk!

 20. Sanagwiririle anapangana chigololo ndi mwini thako mkazi akanakana chigololo panalibe nanga mkaziyo ali kuti poti mamunayonso ndi wamwini amangidwenso naye.

 21. Sanagwiririle anapangana chigololo ndi mwini thako mkazi akanakana chigololo panalibe nanga mkaziyo ali kuti poti mamunayonso ndi wamwini amangidwenso naye.

 22. inu ngati mwasowa nkhani buanj muzingolemba kuti anong’a lero wadyera nyemba

  1. Tsopano ngati atchula DPP chalakwika ndichani uli mbali iti? Zazii kumangodandaula zili zonse wina ali yense amadziwika ndi ntchito yake ma treasurer alipo ambiri uyu ndi wa DPP basi.

  2. Tsopano ngati atchula DPP chalakwika ndichani uli mbali iti? Zazii kumangodandaula zili zonse wina ali yense amadziwika ndi ntchito yake ma treasurer alipo ambiri uyu ndi wa DPP basi.

  3. vuto ndilot akutchula dpp malo osayenera kutchula dpp… nanu chilichose kumangopezerapo mway poti ati dpp…..mmene amapita kumeneko amakakambap za dpp? kapena inali progrmm ya dpp? a2 ogona i dnt see any problm to dis cmnt kti inu mupange rply ka txt kanuko

  4. vuto ndilot akutchula dpp malo osayenera kutchula dpp… nanu chilichose kumangopezerapo mway poti ati dpp…..mmene amapita kumeneko amakakambap za dpp? kapena inali progrmm ya dpp? a2 ogona i dnt see any problm to dis cmnt kti inu mupange rply ka txt kanuko

  5. Mr. #Lesman zinadi kuwiritsa nzeru. Nanga ine olo nkhope ya munthuyo sindiidziwa, olo atamuonesa pachithunzi, mwinanso ngofanana ndi wina? Nkhani za bodza, asaipitse chipani awa.

 23. Pali mwambi wakuti changa changa chinaolera m’thumba,,,,,Nde kumagawana zinthuzi….Umbombo basi….Wanyotsolako ngati?Sanagwililire nde Sindikuonapo Vuto…….Asafuna asiye…..

 24. Pali mwambi wakuti changa changa chinaolera m’thumba,,,,,Nde kumagawana zinthuzi….Umbombo basi….Wanyotsolako ngati?Sanagwililire nde Sindikuonapo Vuto…….Asafuna asiye…..

 25. Ndikhulupilila oyenda ndi Kazi, Amuna a eni ndi ambiri koma mwamulembayu ndichifukwa choti ndi wandale. Ife zandale tatopanawo zingotisaukisabe iya!

 26. Aaa inu atuluka posacedwa uyu kupolice koma akafikile madela ena plz cifukwa iiii

 27. Others really regards screwing as something so special, they would rather lose their dignity for the sake of it. Which pleasure? The one that lasts in seconds? Omg!

 28. Nkhaniyi ayendetse ndi nkhoswe za maanjawa aliyense akanene mavuto make mwina mamunayi muli ana make osati mpaka kumuberekera futi chifu cha aa a police kalondeni kunyumba kwake munthuyi.

  1. zikugwirizana! Aliyense amaziwika ndi zintchito zache! Iyeyo amatchuka chifukwa cha chipani chimenecho! ndiye ngati wapanga zosayenera akuyenera kuti timuziwenso kuzera ku chipanicho! Inu mwaiwala za m’maboma kuti a zibusa amipingo akangopanga chigololo amanenedwa kuti ‘.mbusa wa mpingo wakuti…… Wagwidwa ndi mkazi wa mwini???????

  2. zikugwirizana! Aliyense amaziwika ndi zintchito zache! Iyeyo amatchuka chifukwa cha chipani chimenecho! ndiye ngati wapanga zosayenera akuyenera kuti timuziwenso kuzera ku chipanicho! Inu mwaiwala za m’maboma kuti a zibusa amipingo akangopanga chigololo amanenedwa kuti ‘.mbusa wa mpingo wakuti…… Wagwidwa ndi mkazi wa mwini???????

 29. Kumwenda or Kumwembe? why confusing urself mr reporter boy???? dont be in a rush. be professional. dont you knw that the whole world reads wat u post here???? dont make us Malawians stupid and dumb with ur portrayal of our writing and reporting skills.

 30. Ameneyu popeza ndi wachipani cholamula ndipo malamulo akuwadziwa bwino. Akuyenera kukhala kundende zaka 70 zokha basi. Kuchepera Apo ndekuti aaaaaa!
  Chifukwa mulandu wo fondinga mkazi wamwini ufanana ndi opha munthu. Mkutheka iyeyu Ali nawo mgulu lolandira aja.

Comments are closed.