Caribbean musician Judy Boucher is expected to arrive in the country today ahead of a concert on Sunday.
The artist will perform alongside Lucius Banda on Valentine’s Day at Bingu International Conference centre (BICC) in Lilongwe.
Speaking to Malawi24, Banda who also one of the organisers of the show said they are looking forward to an action packed event in Lilongwe.
Boucher was born in St Vincent in the Caribbean. She released her first solo song titled “Dreaming of little island” which was a hit in the reggae charts in 1985.
So far, she has released 11 albums and seven singles but she is best known for the hit song “can’t be with you tonight”.
Osalowa mgonera mazulo.
Zivute zisavute ndili komko
Zivute zisavute ndili komko
kod mumangotenga akunja bwanji ku Malawi kuno kulibe oyimba? kukhomelera amalawi kumeneko
kkkkkk the prices are so exorbitant,why?kunabwera busy koma sanafike kumeneko. Lucias is not serious.
Lets supot our artists, kod mablacks mungapeleke dat 30000? Why paing fo dis ashawoz show, and it wont b worth it.
Very 9c We Proud Of U Judy I Wil Be There 4 U
Kwa beba kumudziko
Tikavine basi mawa amene tinagula kale matikiti mawa
Ayoyo sojah
Kodi mesa Jody boucher ndi mzungu? Kkkkk
Let me think if i can salel my bicycle or radio 4 show
‘there are more questions than answers’ ‘tears on my pillow’ ‘mr dream maker’ etc
Anakalamba Uyuu.
Good idea
anthu momwe tikuona kuti tiribe ndalama mukuganiza kuti ena alibe? muona kuli anthu ambiri kumeneko
That nite we met yoooo we gonna meet u there Judy i salute u
nice time mama
Tears on my pillow!
Why paying almost R1000 for rubbish!
She is welcome
Ur welcom just use CDs,tizalipirabe basi
Ur welcom just use CDs,tizalipirabe basi
jet plane
jet plane
I am a muslim,chikondwelelo ichi chimanditalikila makamaka kuifunisisa janah
Tikavene bas
he must perform not just playing ma CD akale
Welcome ngakhale tilibe chuma cholowera mu show yanuyo Mr. Boucher
Kodi kumakhala kufuna kutchuka kapena ndi umbuli? Page yomweyi ikalemba za chimanga kuti chafika pa K15000 mumayankhula zoti boma silikuthandi mukuvutika ndi njala. Pano page yomweyi yalemba za show ya K15000 anthu ake nomwenu ovutika ndi njala aja mukuti show yatchipa mukalowa awiriawiri. Shame on you!…..
Judy is great, i love her songs
remove tears on ma pillow
thus de prblm wit we mws, u think if they dont go to the show they ll will buy a bag of maize 4 everyone?
‘maybe i could find a new way to say i love you’ ngati nyimbo iyi sazaimba ndiye asazabweleso
Tears on my pillow we miss this nee
‘some broken hearts never mend’ bwa?!!…..
‘some broken hearts never mend’ bwa?!!…..
Bwanji osafika ku Mzuzu ?
I like Judy she is a legend singer hope our female musican will be inspired by her perfomance and her personality since she performed with Bob Marley and the Wailers
Ndi agogo pono kkkk, agogo oziwa kulongosola chikondi munyimbo
aaa osamutelo artist wanga, photoyo ndiyo yamuonjeza chabe
Welcome mama Judy B 2warm heart of Africa.
Zama cd ayi
Goodshow
Wow !!so sweet i like this lady she really knows how to sing .
Last night we met, tears on pillow, some of her songs touches my heart. Jude long live.
if it is lve my dear welkome to my hme nd we nst the gd tmes together its only one nite.
dont 4get malinga mafia 4 more carrib wit judy
Jb u are welcome
Yanga simuyiona
Pitani mukakumane ndi ma flush disk,, k10,000
Yah!, we do really appreciate 4 hee coming.
Sakayika CD?
Good Dat Ur Here,i Prefer ,sweet Dreams,some Broken Never Mend,thats The Way I Say I Love U,
Paja amabwera udzangoonekela ndikumakuikilani
Ma CD kkkkkkkk!
a bag maize @ k15000 dat a family of 7 can use fo a month nde wina paying k30000/head on da door mmmmm sounds lak of comon sens kkkkk
Ngati ulibe ndalama bwera ndizakulipilira
hahaahaaa u ar right brother..mpaka k30000 kkkkk ine ayi a skeffa chimoto omwewa akwana
Ndalama mulibe amzamu adzikalowa awiri awiri kumeneko ikanakhala ya Makawa mukanapita muzikagenda ndi mabotolo akachasu.
Mavuto sagapatina. Ena ndalama zimenezo ndi chakudya cha 1day. Osaukafe tidikire yathu nthawi
Yap ambiri agula kale ma ticket koma mmmmm enafe kkkkk ndi capital ya business imeneo
Yap ambiri agula kale ma ticket koma mmmmm enafe kkkkk ndi capital ya business imeneo
inu mulinazo?Kapena mukalowera mu ceptic tank kukatulukira mu toilet
kkkk koma gravel ok ndibwera koma ndi transpot yomwetuuu
My fellow Malawians enjoy the show Welcome sister Judy
Pliz Judy use Cds
Welcom Judy i do feel your hits”TEARS ON MY PILLOW,CANT BE WITH U TONIGHT,THAT NIGHT WE MEET,YOU CAUGHT MY EYES” eeesssshh!!!!!! Ndi more fire,all the best,come to BLANTYRE also
is she going to perform live or using cd’s?
She’s welcome to Mzuzu at Salisbury line air conditioned hall.
Good old days .tears on ma pillow. Timalemba mkope nyimbo zake tili pa school ku secondary
ilike her music; including take ur memory when u go That night we met and others!! keep it up Boucher!!
undibwezere change
Mama u r here to remind us good old days
I dont think show ya K30,000 pa head angaike ma CD .Poti soldier wanthuyu ndi nkhalambaso.iyi ndi show ya ma gogo
I dont think show ya K30,000 pa head angaike ma CD .Poti soldier wanthuyu ndi nkhalambaso.iyi ndi show ya ma gogo
If it is love my dear,welcome to my world and let’s share the good times together······
If it is love my dear,welcome to my world and let’s share the good times together······
Welcome Judy
Welcome Judy
hw l wish l wz in mw,,,,,ndikanapita mayi uyu amatha
hw l wish l wz in mw,,,,,ndikanapita mayi uyu amatha
Mayi amenewa amaimba bwino kwambiri
Mayi amenewa amaimba bwino kwambiri
Welcm
Welcm
amaimba nyimbo zanji ine ndi mbuli
amaimba nyimbo zanji ine ndi mbuli
some broken hearts never mend, make ur choice, believe me i would share my love with u, mr dream maker, new way to say i love you, tears on my pillow ++++……many more
some broken hearts never mend, make ur choice, believe me i would share my love with u, mr dream maker, new way to say i love you, tears on my pillow ++++……many more
Wish iwaz dere
Agwiritsa ntchito ma CD?
Agwiritsa ntchito ma CD?
ngati ndipiteko,ndipitila TEARS ON MY PILLOW and THAT NIGHT eeeeeh ine kumva kukoma
ngati ndipiteko,ndipitila TEARS ON MY PILLOW and THAT NIGHT eeeeeh ine kumva kukoma
Mmene kumawawira kulawilira waku ntchito mammawa muja, kukamacha ngati usadzuke nde wina angochoka ukoo kuzatolera za mahala ndi momwe kwacha yagangalamilamu eeee mbambadi umenewo ndi #Mwikhooo… asaaa njala iyi??

Bolani osati bweresera CD,
Bolani osati bweresera CD,
Agogo abwera kudzapanga adopt mwana anga anzao a maradona? kapena kudzalimbikisa mathanyula?
Agogo abwera kudzapanga adopt mwana anga anzao a maradona? kapena kudzalimbikisa mathanyula?
Tikavine zmenez
Tikavine zmenez
Welcome mama, have u brought my pillow
Welcome mama, have u brought my pillow
Ayimba ndi zida kapena flash disk?
wachita bwino kubwera Yudith Botha ndikumbutsile chikale.mzanga weniweni iwe timakhala desk imodzi uku tikukambilana za ‘last night we met’
Kale lake liti?Munthu uli ndi zaka 12
Kkkkkk pa zawana iwe unkakhala mlonda ine abambo kkkkkkkk
koma iwe! iwe! owoh!
pangan,ndinkakuphuzitsa kukwawatu nthawi imeneyotu.udziwa?
Nde abwetsenso memory card…kkk
Its how much. Amandikumbusa chibwezi chiyambilira ujeni
Koma English amalakhula akwelakwela aku Jon eish ngati English yamakaladi kkkkk broken
Kubwera kumalawi atakalamba??? Asaaa
Kubwera kumalawi atakalamba??? Asaaa
Kunotu ndiye ndikuuze iwe kaya amakuti botcha kaya chanichani uko kuli njala ndye ukapusa uzagona osadya.
Am here in jozi to listen music for judy Boucher yuo caught my eyes and l like too much this music for mama Judy
kkkkkkk next year will be kandabongoman sindikuona bho eish!!!!!
u look like a musician lol
u look like a musician lol
kkkkkkkkk mwano
ha ha ha
Is this Judy’s appearance¿ Judy go 2hell
Is this Judy’s appearance¿ Judy go 2hell
Kwao kwa nyimbo za chikondi
Kwao kwa nyimbo za chikondi
Aaaaa February Sakumuona? Azipita Akabwele Tikazagulitsa Fodya

Pitani osungulumwanu. Mwina mungakalaweko kamtendere mmtima akamayetsetsa kukusangalatsani. Ife Christu amatipatsa mtendere. Kusungulumwa ndi HISTORY.
Aaaaa February Sakumuona? Azipita Akabwele Tikazagulitsa Fodya
Aaaaa February Sakumuona? Azipita Akabwele Tikazagulitsa Fodya
Tears on my pillow
crying in the rain
Take your memory with you
Anew way to say ilove u
sweet dreams
Dont break my heart again
That night we met
U close the door
To you isend my love
you caught my eye
dreaming of a little island
turn back the Time
loving me
lovely paradise
turn back the time
eeeeeee ilove this woman akuzifuna nyimbo zakezo hit my inbox
Masinja please do so to me on whats app 0027622626990 if you don’t mind
Ndipange invite 0745004645
Share
Hit mumu
kkk kubweza fees? chimangirizo 100marks
Kkkkkk mwano
Aaaaa Ndifebruary Uyu Muzitithelanso Ndalama, Zipitan Muzabwele Mu April Season Yafodya Ikayamba
kkkkkk ngati sanakutumizeko ku mental ku Zomba akuchedweranji
kandipeleken ndinuyo amwene kkkk
Zabwino zose ku malawiko .
Welkom mam
Malawi,a rubbish pit for de Legends.
this is lucius. #live band
welcome
welcome
who listens to her music anyway. bring artists who matter osat awa akalekalewa. #teambusysignal
Kupepera kusadziwa music inu
sumvera ndiiwe wekha fe timamvera, as the matter of fact stay away frm this concert,,ndizoyenera ife osati ana’nu
hahahhaahahahah basi busy kumamvera zoduka mutu zakalekalezo nanu inu mxieeEwwwww
Aaaa iwe zakale koma zosafwifwa bwanji aise kungoti mwazolowera dance ya 1000 kwacha iyi simungakwanitse inu mulibe ndalama
ndakukweza udindo kuyambira lero ndiwe mbuzi
Kkkkkkkkkkk
Chimidzi chakuchulukila , i can see! its valentine’s day wat do you expect!
when was the last time this JUDY Boucher of yours released an album you guys iyaaaa mbweleratu apa ai
bas busy nd tears on my pillow ndi ine? Foolish
Kkkkkkk
kkkkkkkkkkkkk

Iwe ulibe nkazi nkana sungathe kuziwa music ya judy(mwina ndiwe ka gay)
Iwe ulibe nkazi nkana sungathe kuziwa music ya judy(mwina ndiwe ka gay)
Kkkkk alive dollar awa
Kkkkk alive dollar awa
hahhahahaaha Gray Nantchengwa inuyo nd a stret and yu listen tu stupidity. mediocre
hahhahahaaha Gray Nantchengwa inuyo nd a stret and yu listen tu stupidity. mediocre
BUSY SIGNAL WAKOYO SANGAMAKE PA JUBY-INGOTI PHEE UKAONE MABWANA ENIENI KU DANCE IMENEYI MABIG
BUSY SIGNAL WAKOYO SANGAMAKE PA JUBY-INGOTI PHEE UKAONE MABWANA ENIENI KU DANCE IMENEYI MABIG
hahaahahhahahaha team ma blaks and Skefa madala madala
Show yankhalamba ngat iyi nkoyamba kuiona ine hahahha malodzatu awa
kodi oyimba otchukawa angobwera bwera kuno bwanji?
kodi oyimba otchukawa angobwera bwera kuno bwanji?
Maya Nkhanozga hahahhahahhahah saturdaytu lero
mukukanganirana oyimba?Kkk ndine ma burundi eti?
Asagwiritseso ma cd’s ngati Morgan Heritage
Asagwiritseso ma cd’s ngati Morgan Heritage
welcom to malawi judy
Tears on my pillow
Welkom Apongoz Anga!
Welkom Apongoz Anga!
Kkkkkkkkk
very inspiring singer
very inspiring singer
bola musazalirenso ngati show ya Morgan kuika ma CD! kkkkkkkk
bola musazalirenso ngati show ya Morgan kuika ma CD! kkkkkkkk
Ndiwakonkuno uyu ndasewela naye dzina lake ndi Yudith Botha wa kumsangu
Kkkkkkk Ken msangu wake uti ameneyo?
yemweyi wa pa likumbo msewu wa sengabay
yemweyi wa pa likumbo msewu wa sengabay
wurara thats wow
amalawi mukavina bwanji kumimba kuli njala?
i lov ha songs
Amene ndalama zake alibe nazo chochita apite akabeledwe basi….kkkkkkkk
Ua welcom mama. I lyk ur songs lyk: U caught my eyes, last night we met and Mr dream maker.
She knws hw to sing… Am just worried with her age she is old nw.all the best to you who are attending.
wakuladi pano
#singing:
if it is love, my dear!
welcome to Malawi!
we’ll share the warm hearts!
together!
it’s only one world!
let’s share it together!
na!na!na!na!
na!na!na!na!
#singing:
if it is love, my dear!
welcome to Malawi!
we’ll share the warm hearts!
together!
it’s only one world!
let’s share it together!
na!na!na!na!
na!na!na!na!
Take ur memory with you
@Gravel Masinja:You can say that again! This lady’s exquisite voice sent & still sends several pillows down lovers minds about their special ones that they were or are still dreaming of!
Gogodasi ngati uyu angavine? akufuna kutibera eti?
Gogodasi ngati uyu angavine? akufuna kutibera eti?
wow i wish i could be there but Alas!!nt in mpanje
wow i wish i could be there but Alas!!nt in mpanje
Welcome 2 the warm heart of Africa I lyk ur song ( tears on my pillow ).
Welcome 2 the warm heart of Africa I lyk ur song ( tears on my pillow ).
thats great,i like her songs!
thats great,i like her songs!
Kkkkkkkkk!!!Koma yeah!!!Mukukamuitana atakalamba?
Kkkkkkkkk!!!Koma yeah!!!Mukukamuitana atakalamba?
wow!go and attend it my brothers for as of me ndilibe kalikonse,nayenso kubwera nthawi ya njalayi osabwera cha mma June mu bwanji eishhh but I wish I would be there
wow!go and attend it my brothers for as of me ndilibe kalikonse,nayenso kubwera nthawi ya njalayi osabwera cha mma June mu bwanji eishhh but I wish I would be there
wow!go and attend it my brothers for as of me ndilibe kalikonse but I wish I would be there
wow!go and attend it my brothers for as of me ndilibe kalikonse but I wish I would be there
My my my !!!! Wish i could be their @ her show….she’s simly the best
My my my !!!! Wish i could be their @ her show….she’s simly the best
That nght we met
That nght we met
That nght we met
That nght we met
Thats good
Thats good
Kodi Valentine ya ma Gay imachitika liti?hAhaHaHaHaha Sizokasokonezasoyi ukukuyi kuti show ikathere panjira.
Komaditu
HAhhaHaHah #Clement, iweso sukudziwa???
Kodi Valentine ya ma Gay imachitika liti?hAhaHaHaHaha Sizokasokonezasoyi ukukuyi kuti show ikathere panjira.
Komaditu
HAhhaHaHah #Clement, iweso sukudziwa???
aaaa kusokoneza kulipo man u jst kp waitng
aaaa kusokoneza kulipo man u jst kp waitng
Kikikikikiki #Funny, iyi ya pa 14 siyawo ali ndi tsiku lawo
Kikikikikiki #Funny, iyi ya pa 14 siyawo ali ndi tsiku lawo
ali ndi nyimbo zake andigaire…sindumudziwa uyu sinsinamvereko nyimbo zake so plizZ ndipasenkoni nyimbo za maiWa
+26588190133 Whatsip me wanna give u one of her songs
Ineso ndimaifuna
One best musician during my old school days.
no cds like those thieves who stole our moneys that day
I lov her song, since that nyt i just wanted u
Tears of my pillow…JUDY ur great
Welcome home
mr dream maker Veronica Tungama
Ndukuuza iwe
Nonsense
Pliz we dnt want cd shows in mw make sure you have aband if nt mphwaaaa
Mmalo moti ndalamazo mwatumizile Manolo kumudzi azisangalala ndinjalayi busy kumashow a maCD,,mudzafa imfa yowawa!
Welcome Boucher
Woow!you remind me some of her songs:tears on my pillow n that night we met are my favourite songs.Koma Sizomadzayika Ma CDzijatu ayi.
Musamatumize nkhani zopusa ngat izi plz ngat mwasowa chochita ndibwino muzikacheza ndi achakazanu m’manyumba mwanu.Nkhalamba ngat imeneyi ikufuna chani apa.
Love the artist, welcome hey!
kkk wakula pano,someone sent mi ka video komwe anamujambula in capetown .ndimatsutsa kut its nat her kk
mwatopaeti mpaka chibwezi chapitala kubwela kumalawi heheheeeeeiii zaphweeka
Jolene jolene
Darling Darling …Its Lovely … . .paradise.
wow dats beautiful judy Boucher amatha Mr dream maker
She knows how to sing this lady
Chibwenzi cha Pitala ichi inu nanu kkkkkkkk
tikavine basi akulilongwe akaoneke
She come @ the good time imean the month of lovers. Valentines
Since thaaaaaat night I just wanted you.she is agood singer
Some broken heart neva mend!wow
has she brought her audio cdz to play on stage?
kkkkkkk Morgan style
yah my bro
Yap
Ndi mtsikana uyu kkk wamuona pati kuti ndimgogo kkk
Ndalama za amalawi zimaonedwa zophweka kwambiri… Njala iyi
Khalamba yokonda zi2 lol
welcum
Amalawi mukuwazunzilanji ago go wa , osasiya bwanji azigona .
Kkkkkk gogo wolimbikitsa zachikondi uyu.musiyeni azatilangize kkkk
Was there any publicity?
Ok