Police in Thyolo district are keeping in custody a 21 year-old man who offered his 13 year-old brother for sale.
Thyolo police public relations officer, Edith Kachotsa, identified the man as Samson Phiri and said he was arrested on Tuesday.
According to Kachotsa, Phiri wanted to sell his brother to a businessman for K1 million but the trader alerted officers at Thyolo police station who did not hesitate to arrest the suspect.
Phiri who hails from Ndombole village, Traditional Authority Kapichi in Thyolo district will appear before court soon to answer charges of offering for sale a child contrary to section 82 of child care protection and justice act.
Malawi is one of the countries in southern Africa with high cases of child and human trafficking.
Last month, a couple was arrested in the commercial city of Blantyre for attempting to sell their child in order to raise money to construct a house.
Tamutayeni apa mesa ma bzns akuvuta kodi kwachuluka ndikusowa kwa ntchito kodi mesa bzns yotentha ndi yomwe mukuikananixa lolezani chamba mwina enafe tingapewe kugulitsidwa maka maka azathu achina yellow man mukuwapezerera bwanji
Koma ndiye kwavuta
Ameneyo mutu wake sugwira ntchito bwino.
Aaaa ukuyipitsa mbili yakwathu kukapichi nyapala iwe! Mmangeni zilumika makumi awiri ndi asanu ndikugwila ntchito mwakalavula gaga!!
Business pa mw
zafikapa tigulitsana kwacha ndiyo gwero lazonse
Mulowererepo ambuye
Mulowererepo ambuye
Keep him in custody & auction him when auctioning unclaimed property.
Keep him in custody & auction him when auctioning unclaimed property.
what hell iz dat Goliat Thyolo
what hell iz dat Goliat Thyolo
Sha njala?
Sha njala?
Njala yavuta ngati boma likuti masamba omwewa tizidya kamodzi patsiku so tisagulitse munthu apa?
Njala yavuta ngati boma likuti masamba omwewa tizidya kamodzi patsiku so tisagulitse munthu apa?
Zabodza izi
Zabodza izi
Njala pera iyo mwarengeska malawi
Njala pera iyo mwarengeska malawi
nothing 2 do in Malawi is better 2 sell brotherhood hahahahah! no plans
nothing 2 do in Malawi is better 2 sell brotherhood hahahahah! no plans
Kkkkk koma ziliko
Kkkkk koma ziliko
Why u can’t sale ur president
Why u can’t sale ur president
Mhlomwe uyu waonjeza
Mhlomwe uyu waonjeza
Maludzi patauni
Maludzi patauni
Hehede Malawi Uja Apa Nde Wafikapo
Hehede Malawi Uja Apa Nde Wafikapo
Mwati kwaniiii?
Kwa nansalala ambwiyee
Kkkkk Mapuya mutonena zoona?
Mwati kwaniiii?
Kwa nansalala ambwiyee
Kkkkk Mapuya mutonena zoona?
Mesa yosefe ameyo akufuna kupulumusa anthu ,
Mesa yosefe ameyo akufuna kupulumusa anthu ,
Njala yomweyi
Njala yomweyi
Mzimu wamaganzidwe a umuthu mwa a Malawi wachoka tikumagabiza ngat nyama zakuthengo zoweta bola pena zimamva
Mzimu wamaganzidwe a umuthu mwa a Malawi wachoka tikumagabiza ngat nyama zakuthengo zoweta bola pena zimamva
Kkkkkk kwawo kwa bwana chipuwa kulinso mavuto alomwe umbuli ndimatenda kkkkk
Kkkkkk kwawo kwa bwana chipuwa kulinso mavuto alomwe umbuli ndimatenda kkkkk
Kkkkk iii ayi ndilibe chonena pa malawi watsopanoyu
Kkkkk iii ayi ndilibe chonena pa malawi watsopanoyu
Akayezedwe, mwina ndimisara. Ngati simumupeza nawo matenda amisalawo, kamutsekereni asadzabwelekonso.
hahahahahaha! zoonadi man.
Akayezedwe, mwina ndimisara. Ngati simumupeza nawo matenda amisalawo, kamutsekereni asadzabwelekonso.
hahahahahaha! zoonadi man.
Lilikuti dziko lija?????
Lilikuti dziko lija?????
Malawi24 zanthabwala zanu musamanene zaku THYOLO muzasowa
Malawi24 zanthabwala zanu musamanene zaku THYOLO muzasowa
Kkkkk, ngati uli umphawi, bola ndife ndi umphawi wangawu. Mpaka kufika sayizi imeneyo yongogulitsana? Ngati unanamizidwa, upeze njira zina ayise. Sitifuna zautsiruzo.
Kkkkk, ngati uli umphawi, bola ndife ndi umphawi wangawu. Mpaka kufika sayizi imeneyo yongogulitsana? Ngati unanamizidwa, upeze njira zina ayise. Sitifuna zautsiruzo.
kkkkkkkkkk malawi wanga
kkkkkkkkkk malawi wanga
Tikanena kuti Gay uyu abweretsa navuto kma makani
Tikanena kuti Gay uyu abweretsa navuto kma makani
Kkkkkkkk
Kkkkkkkk
Zafika pogulitsana , let us find better ways of survival, why didn’t he sell himself.
Zafika pogulitsana , let us find better ways of survival, why didn’t he sell himself.
Kkkkkkk
Kkkkkkk
Njala yavuta paliponse mumangoti kumpoto kodi Thyolo ali kuti? Mpaka kugulisana zafika poipa.
Njala yavuta paliponse mumangoti kumpoto kodi Thyolo ali kuti? Mpaka kugulisana zafika poipa.
Kupusa Alomwe kikikikkk
Kupusa Alomwe kikikikkk
I think the idea came from wrong people / devil worshipers, satanist/illuminates
I think the idea came from wrong people / devil worshipers, satanist/illuminates
yaaaaaa! dziko ndi anthu ake tsono.
yaaaaaa! dziko ndi anthu ake tsono.
Is he also from the north?
Yes, Msiska who raped his own daughter is indeed from the North
Is he also from the north?
Yes, Msiska who raped his own daughter is indeed from the North
Malawi 52
Malawi 52
Kikiki dziko lapansi
Kikiki dziko lapansi
Kufuna kutitukwanisa kwa anganyatu kumeneku
Kufuna kutitukwanisa kwa anganyatu kumeneku
No wonder,Zangofika pauchitsiruno,Malawi wathu anali wabwino uyu koma pano ndi Ana Achina,
No wonder,Zangofika pauchitsiruno,Malawi wathu anali wabwino uyu koma pano ndi Ana Achina,
Kodi kuthyolo mavuto alikonso kwawo kwa bwampini kumachitikanso zotelezi eti koma ndiye maluziwa .
Kodi kuthyolo mavuto alikonso kwawo kwa bwampini kumachitikanso zotelezi eti koma ndiye maluziwa .
life in mikuyu or maula prison
life in mikuyu or maula prison
Kkkkkkkk olo ngati panali wina anamunamiza kuti business ndi China chichonse ha ha ha ha koma apa ndiye waonjeza
Kkkkkkkk olo ngati panali wina anamunamiza kuti business ndi China chichonse ha ha ha ha koma apa ndiye waonjeza
Kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk koma Malawi wavuta
Kkkkkkk koma Malawi wavuta
kkkkkkkkkkk no comment
kkkkkkkkkkk no comment
What kind of business is this?
What kind of business is this?
kkkkkk maluzi mpakana kuyamba kusatsana pachibale hahahahh…..ndiyetu february sanati guys ….timva kuti wina wasatsa Big man kkkkkk
hahahahahaha! zoonadi kenako wina agulisa a president.
kkkkkk naneso ndkutha kuziona zitachitika mbambadi dhara kkkk