Musician Fuggie Kasipa has been arrested for being found in possession of an unlicensed gun, Malawi police in Blantyre have confirmed.
According to Blantyre Police Spokesperson Elizabeth Divala the ‘Dale Wanga’ hit maker was arrested today morning.
Divala said Kasipa is currently being kept at Blantyre Police Station and he will appear in court soon for illegal possession of a firearm.
His arrest comes days after police in Salima district arrested two men are in custody for stealing a Greener gun which belongs to Malawi’s renowned Evangelist Shadreck Wame.
It is said that the firearm for the man of God was also not licensed.
Mmangeni Basi
Ndichitetezo mutuluseni ngati sanapheko munthu
You must have four Fuggie! Remember how celebrities are being killed! AK 47 for that matter!
Yense opezeka ndi mfuti opanda chilolezo ndi chigawenga
Does the gun have a crime if not
Uyo usange wananga mulandi tikwendela lamulo ,,,,wakwenela ku yeluzika kwakuyana naunenesko
This z what we call thug life fuggie i salute
Mbava nazonso zanyanya that’s y anthu akupezekanso ndi mfuti pofuna kuzitetezanso komabe licence njofunika Fuggie bro usadandaule ingolipira mlanduwu then ukhale ndi licence••Team Makaveli
Mwati walakwa chaniii? Wapha munthu kapena? Enatu alinazo ndi zitupa zimene koma amagwiritsa ntchito kuba ndi kupha, bwanji mukumangowayang’ana?
Mwati walakwa chaniii? Wapha munthu kapena? Enatu alinazo ndi zitupa zimene koma amagwiritsa ntchito kuba ndi kupha, bwanji mukumangowayang’ana?
Iiiii ok chabwino. Dale wangayo komatu samwa jang’ala. Mpatseni uta wakewo ndi mlenje ameneyo
Iiiii ok chabwino. Dale wangayo komatu samwa jang’ala. Mpatseni uta wakewo ndi mlenje ameneyo
we call poor government malo moti izipanga chitukuko bas kulimbana ndi anthu zowona sugar tizigura 600 kw khara ngat imachoka kuja?musalimbane ndi anthu,inu nyani inu walakwa chani munthu wamulungu kapena wapha ndani inu muziganiza popanga zithu zisilu inu mwava… bwaji kuti muziagwira a amene akupanga za ugey ena mumati right,,,Right yaji imeneyo siusatanic umenewo.
I ve got one also
musiye ndifuna ndizamubwereke kuti ndithanenawo amathanyulawa
AMalawi sadzathekanso mmalo mot Tiziti Chimangen chimenecho koma ayi ndithu , mukuona ngat kut iyeyu anali Mlenje kapena ? Yense wakupexEka ndi Mfut AmAngiwe bas palibe zot ndi Celeb palibe…………………………..Ndakwiya nanu……………………………………….
Is he a murderer?
Pakuti mbala sikudza kuti ikabe koma kupha ndikuononga lamulo ligwile ntchito posatengela mbali malumulowa timapanga tokha sikuti ndiku ameleka kapena kujoni awa ndi akumalawi olo khomo linalililose lili ndi malamulo ake olo Yehova adaika ndondomeko nde apa chigamulo chiyende ngati madzi.ineso ndimamukonda koma apa pokha ndiyendela lamulo.
Ophwanya malamulo aweluzidwe mosayangana nkhope sidzikudziwika mwina amaba kapena ayi poti iyenso ndi munthu
Mukungoyikira Kumbuyo Zoipa. Mitu Yanu Imagwira? Osangokhala Chete Bwanji Kuti Uchitsiruwo Usaonekere? Nonsenu Opanda Okambapo Zanzeru…?! Mxiew! Ikakhala Ya Ma Gay-yo, Mutifunse Ozindikirafe Tikuyankhani!
?
?
Zasangalasa mbuzi kugunda galu,Galu nayenso akati abweze mkumati choka ukafa sudyedwa anthu asapezeke bwanji ndi mfuti sinanga inuyo mukumabwereketsa akuba mfuti zanuza tsono ife tiziziteteza chiyani? Tisiyeni
Zasangalasa mbuzi kugunda galu,Galu nayenso akati abweze mkumati choka ukafa sudyedwa anthu asapezeke bwanji ndi mfuti sinanga inuyo mukumabwereketsa akuba mfuti zanuza tsono ife tiziziteteza chiyani? Tisiyeni
Its sad to see how ppl we are buys kumuyikila kumbuyo coz he is a well known celebrity, and this issue have nothing to do with politics.. Malamulo a Malawi state clearly on the firearm… Ndiye poti umbuli ndiye vuto thats y were busy politisyzng the issue and kumubakila.. Shame.
w nid detonators guns
Congrants to our police,its unlawful to be found with unlicenced gun.such type of people ought to be punished if found guility no matter how popular the offender is,we dont want such nosense to happen,wake up malawians n love our country without considering some political matters
Mh! Wise men speak just because they have something better to say. While Fools speak or make noise because they have to say something though its senseless. Work up Malawi, don’t just argue for the sake of arguing, try to make positive contributions. Let the law of Malawi take its course regardless of one’s status
zachamba mwava ndani kt iye nd wakuba mumasiya zgawenga bwanj mkumalimba nd anthu wamba
True gangster one bullet 4 yo self or4 yo enemies
Apolice ndi okanika kulankhula wanuyo panyapanu ku malawiko.
Mbuzi za anthu.
Iwe betres palibe chomwe ukuziwa ndiwe munthu wa m’kazi.
Ine yanga ndiye simungandilande kuphana kupana basi.
Anthu mukukhala dziko la eni mwayamba kuchangamuka eti? Mumayidziwa mfuti inu kwanu? apatseni ulemu apolice akwanu! Ingakhale mfuti ku dziko. lomwe mukukhalawo simungakagule chifukwa sindiinu ololedwa asaaa mwachangamuka eti. zophunzila kudziko la eni!
Ngat wambanayo muthu mumangen apo bii mumangidwe mlandu onamizla …aimnkatainu agalu osaka.
akanakhala kt mfutiwo anapha nawo mun2 bwenz ndkt mthilen unyolo kma kungopezeka nayo dac not a crime xo plz send him out,,, mukusiya kuwamanga anthu ogulixa chimanga kwa mavenda usiku kwa ADMAC malo mowagulisila anthu oxauka. km mukumanga mu2 ongopezeka nd mft bac a a a a
musiyeni ndi self protection makape inu
umadziwa by yamgaziliro phuuuu bwelekete
The Best Thing Is To Forgive Him Ndikumulangiza Zoyenela Kuchita
Police are rubish
mwasowa chochita mpaka kummanga muthu chifukwa cha mfuti yophera mbalameyo,
Nothing wrong is a weapon to protect himself..fuck all de police!!!! Fuck u tooo
I can now declare that Malawians are not great people. We talk as if we kno what we are talking only to be seen our stupidity by other nationals. How can a person with all five senses back a person found in possesion of a firearm illegally? Yes he is some one we have known for years and he is one of the celebrated guys in music circles but that doesn’t mean he is immune to the law. Am certain everyone would be like ndi chigawenga chimenecho mmangeni if he was someone else. Shame to us!!
apolice kupusa sindingakusekeleleni muyambe amathanyulawo fotseeek! poor work
Yayine ndikozekela ma gay, kuti ndidzathile machaka mmatako. Ngati mmene ndimathilila agwape kumtchile thawi ya usiku. Shoot to kill malawi gays. No hopeless to gays sexuality.
pepani amuzikishani muchira.
Monga yayineso mudzalanda mr Malawi government?
Protocol, chimidzi bwanji
Anzanu amayeza mfuti ngati zimenezo ku theba timagula kushop wen police found u with it amangoyeza then ngati inapha muthu they arrest u
ur a liar which south africa? try today to have un licenced gun even if it hasnt been used to see if u will last 2months with it.any one with unlicensed gun when found in SA saves a maximum of 15months in prison. so osawanamiza anthu za joni ngati muli nokha mu joni muno akulu. am sure simuzanamanso
Machende amako ndati amayesa yet udont get it wat happen with fugi nyini yamako galu iwe
ali ufuna uzitinamiza et?kkkkkkkk
Ma coment achuluka pano ngama suspect okhaokha!Enanu sanakupezenponi akuba a mfuti,,mutha kudzalola mbavayo kuchinda mkaz wako iwe kumaonerera nd2,,,,muzaziona!!
Ma coment achuluka pano ngama suspect okhaokha!Enanu sanakupezenponi akuba a mfuti,,mutha kudzalola mbavayo kuchinda mkaz wako iwe kumaonerera nd2,,,,muzaziona!!
Malo molesa kape akubwerayo mwayamba kuwapana mitu ma citizen za ziiii
If he break the law he must be charged don’t bring issue of homosexual at anytime so u mean they must leave all law breakers & just focus on homosexual? Dont play cheap politics guys
Mpatseni volovolo wake munthuyu..iye ali ndi machine opangila mfuti? mesa munamugulitsa nokha…mukufunaso mumukawe koma yaah!!
Ati mfut inalibe COF kapena insurance? Kk
Apolisi nanuso serious zomwezi murine ntchito yina
Ine ndichizulu chokha lamaphoiisa babamba fugie kasipa woke wayasklanya umunthu mala une sibamu abanandaba kati inii ikinga? Bamalawi lo munthu muphumisseni manjesoo. Yebo
Ine ndichizulu chokha lamaphoiisa babamba fugie kasipa woke wayasklanya umunthu mala une sibamu abanandaba kati inii ikinga? Bamalawi lo munthu muphumisseni manjesoo. Yebo
FUGI SANALAKWITSE AMAKHALA OKONZEKA NGATI MTSILIKALI WENIWENI. KUMAKHALA NDI CHIDA NKWABWINO. APOLISI NSO INU MUKUMVA ZOTI MAGUFULI AKUFUNA KULANDA NYANJA KOMANSO MA GAY AWA NDIYE MMATI KASIPA FUJI ANGOKHALA OSAKONZEKA.
FUGI SANALAKWITSE AMAKHALA OKONZEKA NGATI MTSILIKALI WENIWENI. KUMAKHALA NDI CHIDA NKWABWINO. APOLISI NSO INU MUKUMVA ZOTI MAGUFULI AKUFUNA KULANDA NYANJA KOMANSO MA GAY AWA NDIYE MMATI KASIPA FUJI ANGOKHALA OSAKONZEKA.
Zazii ntayeni ameneyo kagwileni mbava
Zazii ntayeni ameneyo kagwileni mbava
Kkkk kulusatu anthu
Kkkk kulusatu anthu
manyi anu mwamva mbwezeleni mfutiyo mwiniwache ndipo asakalowe kundende apo biiiii muzifa mmozimmozi. zikakhala za mifuti kumalawikuno tsopano 70%
manyi anu mwamva mbwezeleni mfutiyo mwiniwache ndipo asakalowe kundende apo biiiii muzifa mmozimmozi. zikakhala za mifuti kumalawikuno tsopano 70%
Mulimbane ndi Tanzania uku nyanja yathu yapita…….
Inu munkadikila tsiku lalero zaka zonsezi ‘opepela ‘opepela ‘opepela ‘opepela, akatuluka akuyimbani trust me!
Inu munkadikila tsiku lalero zaka zonsezi ‘opepela ‘opepela ‘opepela ‘opepela, akatuluka akuyimbani trust me!
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Mukamulanda kut mwaykonda tmtumzla ynaxo mwamva alonda ynu
Mukamulanda kut mwaykonda tmtumzla ynaxo mwamva alonda ynu
Amene walanda mfutyo mbolo yake
Amene walanda mfutyo mbolo yake
Give it back to Fuggie a gun its for protection and free him as well go and blow lesbians,gays as well as bisexuals not this nonsense…….!!
Give it back to Fuggie a gun its for protection and free him as well go and blow lesbians,gays as well as bisexuals not this nonsense…….!!
Even corruption iz ryzing up bcoz ov the police! Wht knd ov mada hs the man done wth the gun??? Jst liv hm!!.
Even corruption iz ryzing up bcoz ov the police! Wht knd ov mada hs the man done wth the gun??? Jst liv hm!!.
Osamanga osoka nsapato amene ali ndi zida zoopsya bwanji koma kunyengana peter ndi peter basi musiyeni ufulu tinasankha mwayambanso nkhaza panya panu
Osamanga osoka nsapato amene ali ndi zida zoopsya bwanji koma kunyengana peter ndi peter basi musiyeni ufulu tinasankha mwayambanso nkhaza panya panu
Nawenso
That Gun Ukuyenela Kufufuzidwa Mwina Amagwirisa Ntchito Kupangila Zachiwembu
Apolice tatopa nanu choti mdziwe mfuti masiku ano ndi londa wapa nyumba ku muzingo mangapotu ngati ndi maluzi mwalusa nawomukukanika kumnga anthu omwe anathyora maofface aboma amene anatenga ndalama zankhaninkhani mitu yose ya malawi ikuvutika pano mkumanga munthu amene ali nigalu wake pakhomo kupusa kwa apolice…
eti a Mozy chilungamo chilipo apa?
Apolisi tibwere kapena mubwela¿?
Apolisi zomwezi mpaka kutengela hard
Tikamachoka ku jonz kuno tizibwelesadi,a police enanu tizakuthyolani akatumba dikilani
Nd then??
Zikomo
Papita nthawi asanatulutse chimbale ndiye amaopa kuti mumuiwala .
Ichi ndiye chimbale chomwe watulutsa.
Osakam’manga m’busa uja bwanji?
apolice mutayen amene azipanga zake ameneyo
apolice mutayen ape
I hav a bomb
Mbuzi Za police anyamata Ovina Beni.alonda abakha enieni.
Apolic munazwa bwanj kut alindmfut iyeyo
……??
Zamkutu mukulephera kugwira a cashgate gv hm bc hs property
money talks you are de 1 give him de gun che officer tangokambiranani bwinobwino za ndalama mumafuna kupasanazo wosatisokosa
musiyeni 50 cent wathu ,mwamulanda mesa ife timutumizirano bazuka aphuritse ausilu nose
tamangolimbanani ndi mavuto azanjalawa mukulimbana ndifuti yodzitetezera anawopseza nawo ndani wapha ndani musiyeni fuji kwake mkusangalatsa anthu ndi ndidaliwangayooo
amalawi nanu mwasowa ntchito eti mmalo molimbana ndi umphawi ndi njala yomwe yamveka padziko lonse lapansiyo mukulimba ndizinthu dzaziiiiiiiiiiiiiiii
No comment
Malo momagwira akukwatirana akazi kapena amuna okhaokha ndikumawapha kuti zisapitilire muli bzy kulimbana ndi anthu apheee futiyo waphanayo ndani mmamizimu muli mifuti yambiri mbiri anthu onsewa akumalowa jozwa ndiye mumati mwasowa zochita kapena mumumasule komanso mfuti wake mumubwezere zachamba ayi usilu bas koma akanati mathanyula ndiye kukondwa mumuuzenso TEMBENU wanuyo asamale
Malo momagwira akukwatirana akazi kapena amuna okhaokha ndikumawapha kuti zisapitilire muli bzy kulimbana ndi anthu apheee futiyo waphanayo ndani mmamizimu muli mifuti yambiri mbiri anthu onsewa akumalowa jozwa ndiye mumati mwasowa zochita kapena mumumasule komanso mfuti wake mumubwezere zachamba ayi usilu bas koma akanati mathanyula ndiye kukondwa mumuuzenso TEMBENU wanuyo asamale
Muzakhale Mtsogoleri Inuyo Muzizalekerela Anthu Akuyenda Ndi Mfuti
Mfuti yophera mbalame yomweyi mpaka kuchotokosi?..kkkkkkkkk..koma mathanyula kumero kwanuko mbeeeeeee…
Eeeee ndiyophera anyani ati bweeeewaaa atulusidwe mwachangu
Atuluka iye siwakuba
Fuggie sanalakwise kukhala ndi mfut.kod cholinga chake chosunga mfut inu mukuziwa? Bwelaniso muzandimange ine bola iye ali ndi mfut imozi koma ine ndi 52 ton.(52 ton of gun)
Hahaaah akapokola if u knw ur job well,,arrest Peter da Homosexual..
Musiyeni Fuggie,,,,a gun z a property
Koma Malawi,,Hvng a property z nw a crime
KAMUZU Banda come back
Ooh zoopsa2
Ine yanga pamene ndikunena pano ili nyumba ,mudzayerekeza kutenga yanga ndidzakucotsani mphuno
police themselves are thiefs,,,stealing by using government guns…live him alone malawi police mumasowa zochita eti
Nothing wrong there,just give him his machine,he want to shoot all those who steal money in government and those cashgate,also he want to shoot those they talk nosense in pariament instead talking about development mpatseni machine ake wakwiya mwini malawi alanda ufumu akufuna ayeseko naye onsewo kuyambira ABCD alephera.
zaziii
Munthu wotchuka ngati uyu …sangamangoyenda wopanda Chitetezo…even inuyo mukuzitcha kuti aPolice nu Mukumudziwa uyu kuti ndi woyimba Siwakubayi….koma kakaka kumukakamila shaaaaa.Mukungolimbana ndi wanthu wosalakwa Dzimbalangondo dzukukanikani kuzigwira Kuopa…Nanga uja wasendedwa Mutu uja mwampeza wapanga izi???
Mubweleso Muzandimange Ine.Bolani Iye ali ndi mfuti,koma ine ndili ndi;chikwanje,nkhangwa,legeni,uta,hamala,,Nde mukulimbana ndimunthu oti ali ndichida chimodzi
Dale wangayo e samwa jang’ala…sapha munthu. .
Release him
Jelousy
I think he bought it for his security.
mfuti izipexzeka ndiazibusa fuggie ndindani..
Wapha nayo ndani?
Akadaphera muthu tikadati mmangenidi
Akuti yopanda mapepalatu ndiye pagona khani futi ndiyake
Apolice mwasowa chochita eti mbamva inu bwezani mfuti kwamwini wake yake siyophela munthu koma yozitetezela kwa mbava ngati inu anthu opusa mwapanga bwanji
dats for personal security i guess,za zii anthu akufa njala kuno!!
M’bwezereni munthu gawo lachuma chake!
for protection palibe nkhani.
Shame on you a police athu.Mukulimbana ndi kumanga innocent pple pomwe mbava zili m’boma mwanu momwemo zikudyerera mwaufulu.Akutumani eti?
idont c the problem.We have notorious thugs even the police themselves know did they here anything bad of him?
All I can say is “get out soon bro” and at least licence it if you won’t get a ban to do one
Hemmmmm why fuggie?
Mzati Mannah
Ndimulenje amaphera nyama mfutiyo musamukhomelele mupatseni
Kumeneko nde kukondera tiziti fujiyo alibe ufulu okhala ndi mfuti? Amabungwe mulikuti apa? Ma donors mulikuti? Awa amathanyula akamangidwa nde mudziti akuaphwanyira ufulu zopusa uchitsiru God wu punish anthu oipainu mumati mumamenyera ufulu wamunthu bwanji osamumenyera ufuluwake fuji?
Ndi ana amu Ndix
Ama user for protection palibe vuto apa
Esh! Another story
Tampatsani zitsiru inu fut yake muthuyo inu mulibe
Fuggie morefire
Mphamvu ya maluz panyasaland.
Koma muzimulora kusuta amakonda chilengedwe tu
Kkkkkkkkkkk
Akuchalira kuthana ndi Tanzania mpasen machine akewo basi.
Amangidwe bansi wachwembu ameneyo eeet.
no body knows about tomorrow mr you can be the next nziko ili