Musician Fuggie Kasipa arrested for possessing a gun

Advertisement
Fuggie Kasipa
Fuggie Kasipa
Fuggie Kasipa; Arrested.

Musician Fuggie Kasipa has been arrested for being found in possession of an unlicensed gun, Malawi police in Blantyre have confirmed.

According to Blantyre Police Spokesperson Elizabeth Divala the ‘Dale Wanga’ hit maker was arrested today morning.

Divala said Kasipa is currently being kept at Blantyre Police Station and he will appear in court soon for illegal possession of a firearm.

His arrest comes days after police in Salima district arrested two men are in custody for stealing a Greener gun which belongs to Malawi’s renowned Evangelist Shadreck Wame.

It is said that the firearm for the man of God was also not licensed.

Advertisement

154 Comments

 1. Uyo usange wananga mulandi tikwendela lamulo ,,,,wakwenela ku yeluzika kwakuyana naunenesko

 2. Mbava nazonso zanyanya that’s y anthu akupezekanso ndi mfuti pofuna kuzitetezanso komabe licence njofunika Fuggie bro usadandaule ingolipira mlanduwu then ukhale ndi licence••Team Makaveli

 3. Mwati walakwa chaniii? Wapha munthu kapena? Enatu alinazo ndi zitupa zimene koma amagwiritsa ntchito kuba ndi kupha, bwanji mukumangowayang’ana?

 4. Mwati walakwa chaniii? Wapha munthu kapena? Enatu alinazo ndi zitupa zimene koma amagwiritsa ntchito kuba ndi kupha, bwanji mukumangowayang’ana?

 5. we call poor government malo moti izipanga chitukuko bas kulimbana ndi anthu zowona sugar tizigura 600 kw khara ngat imachoka kuja?musalimbane ndi anthu,inu nyani inu walakwa chani munthu wamulungu kapena wapha ndani inu muziganiza popanga zithu zisilu inu mwava… bwaji kuti muziagwira a amene akupanga za ugey ena mumati right,,,Right yaji imeneyo siusatanic umenewo.

 6. AMalawi sadzathekanso mmalo mot Tiziti Chimangen chimenecho koma ayi ndithu , mukuona ngat kut iyeyu anali Mlenje kapena ? Yense wakupexEka ndi Mfut AmAngiwe bas palibe zot ndi Celeb palibe…………………………..Ndakwiya nanu……………………………………….

 7. Pakuti mbala sikudza kuti ikabe koma kupha ndikuononga lamulo ligwile ntchito posatengela mbali malumulowa timapanga tokha sikuti ndiku ameleka kapena kujoni awa ndi akumalawi olo khomo linalililose lili ndi malamulo ake olo Yehova adaika ndondomeko nde apa chigamulo chiyende ngati madzi.ineso ndimamukonda koma apa pokha ndiyendela lamulo.

 8. Mukungoyikira Kumbuyo Zoipa. Mitu Yanu Imagwira? Osangokhala Chete Bwanji Kuti Uchitsiruwo Usaonekere? Nonsenu Opanda Okambapo Zanzeru…?! Mxiew! Ikakhala Ya Ma Gay-yo, Mutifunse Ozindikirafe Tikuyankhani!

 9. Zasangalasa mbuzi kugunda galu,Galu nayenso akati abweze mkumati choka ukafa sudyedwa anthu asapezeke bwanji ndi mfuti sinanga inuyo mukumabwereketsa akuba mfuti zanuza tsono ife tiziziteteza chiyani? Tisiyeni

 10. Zasangalasa mbuzi kugunda galu,Galu nayenso akati abweze mkumati choka ukafa sudyedwa anthu asapezeke bwanji ndi mfuti sinanga inuyo mukumabwereketsa akuba mfuti zanuza tsono ife tiziziteteza chiyani? Tisiyeni

 11. Its sad to see how ppl we are buys kumuyikila kumbuyo coz he is a well known celebrity, and this issue have nothing to do with politics.. Malamulo a Malawi state clearly on the firearm… Ndiye poti umbuli ndiye vuto thats y were busy politisyzng the issue and kumubakila.. Shame.

 12. Congrants to our police,its unlawful to be found with unlicenced gun.such type of people ought to be punished if found guility no matter how popular the offender is,we dont want such nosense to happen,wake up malawians n love our country without considering some political matters

 13. Mh! Wise men speak just because they have something better to say. While Fools speak or make noise because they have to say something though its senseless. Work up Malawi, don’t just argue for the sake of arguing, try to make positive contributions. Let the law of Malawi take its course regardless of one’s status

 14. Anthu mukukhala dziko la eni mwayamba kuchangamuka eti? Mumayidziwa mfuti inu kwanu? apatseni ulemu apolice akwanu! Ingakhale mfuti ku dziko. lomwe mukukhalawo simungakagule chifukwa sindiinu ololedwa asaaa mwachangamuka eti. zophunzila kudziko la eni!

 15. Ngat wambanayo muthu mumangen apo bii mumangidwe mlandu onamizla …aimnkatainu agalu osaka.

 16. akanakhala kt mfutiwo anapha nawo mun2 bwenz ndkt mthilen unyolo kma kungopezeka nayo dac not a crime xo plz send him out,,, mukusiya kuwamanga anthu ogulixa chimanga kwa mavenda usiku kwa ADMAC malo mowagulisila anthu oxauka. km mukumanga mu2 ongopezeka nd mft bac a a a a

 17. I can now declare that Malawians are not great people. We talk as if we kno what we are talking only to be seen our stupidity by other nationals. How can a person with all five senses back a person found in possesion of a firearm illegally? Yes he is some one we have known for years and he is one of the celebrated guys in music circles but that doesn’t mean he is immune to the law. Am certain everyone would be like ndi chigawenga chimenecho mmangeni if he was someone else. Shame to us!!

 18. Anzanu amayeza mfuti ngati zimenezo ku theba timagula kushop wen police found u with it amangoyeza then ngati inapha muthu they arrest u

  1. ur a liar which south africa? try today to have un licenced gun even if it hasnt been used to see if u will last 2months with it.any one with unlicensed gun when found in SA saves a maximum of 15months in prison. so osawanamiza anthu za joni ngati muli nokha mu joni muno akulu. am sure simuzanamanso

 19. Ma coment achuluka pano ngama suspect okhaokha!Enanu sanakupezenponi akuba a mfuti,,mutha kudzalola mbavayo kuchinda mkaz wako iwe kumaonerera nd2,,,,muzaziona!!

 20. Ma coment achuluka pano ngama suspect okhaokha!Enanu sanakupezenponi akuba a mfuti,,mutha kudzalola mbavayo kuchinda mkaz wako iwe kumaonerera nd2,,,,muzaziona!!

 21. If he break the law he must be charged don’t bring issue of homosexual at anytime so u mean they must leave all law breakers & just focus on homosexual? Dont play cheap politics guys

 22. Ine ndichizulu chokha lamaphoiisa babamba fugie kasipa woke wayasklanya umunthu mala une sibamu abanandaba kati inii ikinga? Bamalawi lo munthu muphumisseni manjesoo. Yebo

 23. Ine ndichizulu chokha lamaphoiisa babamba fugie kasipa woke wayasklanya umunthu mala une sibamu abanandaba kati inii ikinga? Bamalawi lo munthu muphumisseni manjesoo. Yebo

 24. FUGI SANALAKWITSE AMAKHALA OKONZEKA NGATI MTSILIKALI WENIWENI. KUMAKHALA NDI CHIDA NKWABWINO. APOLISI NSO INU MUKUMVA ZOTI MAGUFULI AKUFUNA KULANDA NYANJA KOMANSO MA GAY AWA NDIYE MMATI KASIPA FUJI ANGOKHALA OSAKONZEKA.

 25. FUGI SANALAKWITSE AMAKHALA OKONZEKA NGATI MTSILIKALI WENIWENI. KUMAKHALA NDI CHIDA NKWABWINO. APOLISI NSO INU MUKUMVA ZOTI MAGUFULI AKUFUNA KULANDA NYANJA KOMANSO MA GAY AWA NDIYE MMATI KASIPA FUJI ANGOKHALA OSAKONZEKA.

 26. manyi anu mwamva mbwezeleni mfutiyo mwiniwache ndipo asakalowe kundende apo biiiii muzifa mmozimmozi. zikakhala za mifuti kumalawikuno tsopano 70%

 27. manyi anu mwamva mbwezeleni mfutiyo mwiniwache ndipo asakalowe kundende apo biiiii muzifa mmozimmozi. zikakhala za mifuti kumalawikuno tsopano 70%

 28. Give it back to Fuggie a gun its for protection and free him as well go and blow lesbians,gays as well as bisexuals not this nonsense…….!!

 29. Give it back to Fuggie a gun its for protection and free him as well go and blow lesbians,gays as well as bisexuals not this nonsense…….!!

 30. Osamanga osoka nsapato amene ali ndi zida zoopsya bwanji koma kunyengana peter ndi peter basi musiyeni ufulu tinasankha mwayambanso nkhaza panya panu

 31. Osamanga osoka nsapato amene ali ndi zida zoopsya bwanji koma kunyengana peter ndi peter basi musiyeni ufulu tinasankha mwayambanso nkhaza panya panu

 32. That Gun Ukuyenela Kufufuzidwa Mwina Amagwirisa Ntchito Kupangila Zachiwembu

 33. Apolice tatopa nanu choti mdziwe mfuti masiku ano ndi londa wapa nyumba ku muzingo mangapotu ngati ndi maluzi mwalusa nawomukukanika kumnga anthu omwe anathyora maofface aboma amene anatenga ndalama zankhaninkhani mitu yose ya malawi ikuvutika pano mkumanga munthu amene ali nigalu wake pakhomo kupusa kwa apolice…

 34. tamangolimbanani ndi mavuto azanjalawa mukulimbana ndifuti yodzitetezera anawopseza nawo ndani wapha ndani musiyeni fuji kwake mkusangalatsa anthu ndi ndidaliwangayooo

 35. amalawi nanu mwasowa ntchito eti mmalo molimbana ndi umphawi ndi njala yomwe yamveka padziko lonse lapansiyo mukulimba ndizinthu dzaziiiiiiiiiiiiiiii

 36. Malo momagwira akukwatirana akazi kapena amuna okhaokha ndikumawapha kuti zisapitilire muli bzy kulimbana ndi anthu apheee futiyo waphanayo ndani mmamizimu muli mifuti yambiri mbiri anthu onsewa akumalowa jozwa ndiye mumati mwasowa zochita kapena mumumasule komanso mfuti wake mumubwezere zachamba ayi usilu bas koma akanati mathanyula ndiye kukondwa mumuuzenso TEMBENU wanuyo asamale

 37. Malo momagwira akukwatirana akazi kapena amuna okhaokha ndikumawapha kuti zisapitilire muli bzy kulimbana ndi anthu apheee futiyo waphanayo ndani mmamizimu muli mifuti yambiri mbiri anthu onsewa akumalowa jozwa ndiye mumati mwasowa zochita kapena mumumasule komanso mfuti wake mumubwezere zachamba ayi usilu bas koma akanati mathanyula ndiye kukondwa mumuuzenso TEMBENU wanuyo asamale

 38. Fuggie sanalakwise kukhala ndi mfut.kod cholinga chake chosunga mfut inu mukuziwa? Bwelaniso muzandimange ine bola iye ali ndi mfut imozi koma ine ndi 52 ton.(52 ton of gun)

 39. Nothing wrong there,just give him his machine,he want to shoot all those who steal money in government and those cashgate,also he want to shoot those they talk nosense in pariament instead talking about development mpatseni machine ake wakwiya mwini malawi alanda ufumu akufuna ayeseko naye onsewo kuyambira ABCD alephera.

 40. Munthu wotchuka ngati uyu …sangamangoyenda wopanda Chitetezo…even inuyo mukuzitcha kuti aPolice nu Mukumudziwa uyu kuti ndi woyimba Siwakubayi….koma kakaka kumukakamila shaaaaa.Mukungolimbana ndi wanthu wosalakwa Dzimbalangondo dzukukanikani kuzigwira Kuopa…Nanga uja wasendedwa Mutu uja mwampeza wapanga izi???

 41. Mubweleso Muzandimange Ine.Bolani Iye ali ndi mfuti,koma ine ndili ndi;chikwanje,nkhangwa,legeni,uta,hamala,,Nde mukulimbana ndimunthu oti ali ndichida chimodzi

 42. Shame on you a police athu.Mukulimbana ndi kumanga innocent pple pomwe mbava zili m’boma mwanu momwemo zikudyerera mwaufulu.Akutumani eti?

 43. Kumeneko nde kukondera tiziti fujiyo alibe ufulu okhala ndi mfuti? Amabungwe mulikuti apa? Ma donors mulikuti? Awa amathanyula akamangidwa nde mudziti akuaphwanyira ufulu zopusa uchitsiru God wu punish anthu oipainu mumati mumamenyera ufulu wamunthu bwanji osamumenyera ufuluwake fuji?

Comments are closed.