The Malawi national football team and Mighty Wanderers shot-stopper has signed a one year contract with Mozambican top division side Chingale FC, Malawi24 has learnt.
Richard Chipuwa left the country for Mozambique last week for trials without the consent of his parent club where he impressed and was offered a one year deal worth K3.6 million.
However, Wanderers have reacted angrily towards the news saying its an abormination for the player to be offered a contract without the knowledge of his parent club. “What we know is that Richard is our player.
”His contract with us will run up to 2018 and we are surprised to hear that he has been offered a one year deal else where without our consent.”
“I have never seen a club without discipline like Chingale FC and let me be clear, he won’t get any clearance from us if he thinks that he is clever. We are waiting to see him arriving for pre-season training next month,” said Nomads general secretary Mike Butao.
He also revealed that the player never informed them of his decision to travel to Mozambique. Chipuwa made it clear at the end of last season that he was looking for a new challenge away from Lali Luban where he has been playing since 2006.
Chipuwa Waiwala Zomwe Ampangila A Wanderers
Malonda abwino sasowekera kutsatsa
nyelele zimadzi kkkkkkkkkkk
all the best chipuwa,,,,, happy for yu
amativutitsa ameneyo makamaka ikafika nthawi ya mapenate yenda bwino chipuwa abale akowa chaka chino ndi choti tiawonetse zilango awadziwe mapale mawule woyeee
Ma players aku Malawi school mulibe they need guidance just look what happened to Gaba they jump into conclusion
Ndangomvetsedwa kuti ku club house kunali kulira ngati maliro kutangomveka kuti chipuwa wakhoza Ma trials.
khani yosamveka iyi ,muthu mene amapita anapelekeza awanderes omwewo dzose amakambilana ndi team ,lero wakhoza akunenanso kuti contract inali isanathe shupit malawi dzuka
Chipuwa should follow procedures.He is a good goalkeeper.He has assisted Mighty.Let him go.Manoma mwanyanya,muzichinya.Mumangopasirana basi?
Kkkkkkk……akumuthawa Jaffarie Neymar Chande, game iliyonse kumudya plain-plain
Apite Mulungu Atipatsa Wina Wabwino Goal Boy.
Chipuwa Sanaganizile Zacontract Ku Wanderers
wishing him the best of success!
If he is signing the contract with the Mozambique club SECRETLY then something is seriously wrong with that arrangement. He knows he has unfinished business with his former club and he is only making life difficult for himself. He just have to follow procedure and not cut corners
Izi ndizosiyilana abale anga ena alowe ndipo ena atuluke ndiye kukhalakotu. Chimodzimodzi ground ena amalowa akasewela ena amatulusidwa chachilendo ndichiyani pamenepa? Kuzolowela kubwekela basi shi i i iya!
kkkkk zangovuta kut wacoka mwa mnjira yke kmaxo Noma imazikonda kuyankhura kwambir player akacoka,tidzit mumafuna cani?
Mulekeni apite he is looking for green pastures
Chipuwa needs to be desciplined! Thus not the way to go! Mr Butao, give him a lesson so that other players should learn to follow procedures period!
Kungochoka player m’modzi basi wewe wewe wewe musatero inu bwanji? Team ndiyayikulu iyi.
Yaboooka Nde ngati Mzuni inadyamo 3 – 0 alipo pande kayaaaaaa kkkkk Ine wanga Kumkwawa alipo osaiwala Chaima mbali inayi Vincent kkkkkk basitu yaboooka
Ambiri mukulemba apa malamulo ampira mukuoneka simumawamvetsetsa. Kodi team ya ku Mozambique idabwera kuti ikufuna Chipuwa ku Wanderes kuti akayese mwai kwao? Kapena ili ndi owaimira kuno monga mmene ali Kondi Msungama kapena Ben Chiwaya kuti akhonza kuyamba zokambirana. Wanderes singakondwe kuti anyamata ake azichoka mopanda kutsata malamulo. Ngati mukuwadziwa malamulo ampira kumbukirani kuno kuli WINDOW TRANSFER, kodi matimu athu akutsata ndondomeko yanji pogulitsana osewera. Football is a short term career, ndiye Chipuwa adziwe kuti mtsogolo mwabwino mmbuyo mwabwino ntchentche inatero. Chonde a Wanderes amulore apite coz ndi tsogolo lake komabe amuunikire malamulo amati chiani? Musaiwale kuti Chipuwa anakhala goalkeeper wodalilika pambuyo pakuchoka kwa Simplex Nthala kupita ku Mozambique komwe tikukambaku.
Ndiye kumatumbwa ndi 1.3 ya sponsor wasiyatu kachenjeko kkkkk
Kaya zanu izo…kkkkkkkkk @ neba..
Musiyeni avaye ameneyo nanga mkutani timukakamile abetsa ma game mapeto ake
Timu singaonongeke chifukwa choti Chipuwa wachoka ayi wanderes inalipo ilipo izakhalako popanda Chipuwa uyende bwino star zabwino zonse God be with u ndalama yapaMalawi sikinunkha kanthu
kkkkkk koma chaka chino wina alila,team yonse ya nyelere amene amaonekako ngati mwina amaativuta ndi ameneyi,kkkk apa ndiye zavuta baasi yenda bwino ayise kasake ndalama kumeneko ife kuno tiwakunthe abale akowa
Munkutha chingambwe fc osati noma
kkkk noma yomweyo pajat ku pre season mumasewela ndi chinangwa madrid mukawina mkumanamizana kuti muli bwino kkkkk wandaz chaka chino ndi yabooooka kkkk
time z the best doctor, lets wait n see
time z the best doctor, lets wait n see
Kuchoka sachoka chomcho,… Even pakhomo umasazika abale… Man chipuwa mwandikhumudwitsa unless ngat pali ma problm ena poti tamva mbali imodzi
if its secret how did you get to know about his privacy lol….
Am one of wondrers spoterz but to say de truth let him go coz dats his future no matter what procedure let me say go man anthu ena anazolowera kumapepha kenako azikapeza chokamba kubawo sowani man kadyeni Bakayao mukaone kusinthabasi
akachoka choncho player wa bullets ndi mbuli. .kkk
Musiye ayende, Kasiye kayende, chisiye chiyende asiye ayende, dzisiye dziyende
Muloleni apite basi
Ngati club sikumuthandiza atani?Mpaka akalambile ku Malawi komko osakaona zina bwanji.Enanu mukuti adzakulila mmampatsa chani? Ok olo zitakhala kuti wabwele ku Malawi team Noma yokha adzamtenga ena pita m’bale R. Chipuwa.
Mneba wayendedwa njomba ndimwana wanyumba momwemo. Hhhhhhhhhhhhhhhhhh. Iye wasata komwe kuli chilembwe.
Khani si khaza koma ndondomeko yomwe wasata sinayende bwino team imayamba kukamba ndi team izake then go ahead ndi prayer . Team ikabwela ndikunvana nayo khani kwacha apita ndi songolo lake, jimmy anachoka bwanji
Who bewitched him.chipuwa,please follow the procedures u are such a good player.
#rich kaone zina…pamalawi palibe dollar…kumangobwera pa holiday…
#rich kaone zina…pamalawi palibe dollar…kumangobwera pa holiday…
Amalawi mtima wankhaza tieni tileke ngati wapeza mwai chipuwa muloreni apite osamapanga choncho
I hear wanderers r not aware of dat, no wonder dats malawis futbot w very blind
he is ryt ngati ndiukaidi
ndengati ili SECRETELY iweo wadziwa bwa?
zaboza zoti zasecret nzoziwikiratu tinayamba nkale kumva zoti akupita ku moshko
Ayende basi tipeza wina azatidandaula kuti tamueskera mwai koma osamachoka choncho kwanu nkwanu
Muliranso Chani Inuuu8?Akufuna Ndalama Chipuwa
Muliranso Chani Inuuu8?Akufuna Ndalama Chipuwa
neba sanachite bwino ndithu
Kaone zina m’bale bas