A 29 year-old Malawian man in Ntchisi has been handed a 10-year jail term for stealing maize and stabbing the owner with a sharp knife.
Police in Ntchisi nabbed the man, Hejasi Tchale, after he was suspected of stealing maize belonging to Jonasi Sitola and stabbing him seven times on the arm.
According to police, the incident happened on the night of 17 November this year when the convict went to the house of Jonasi and stole a bag of maize. After hearing a strange sound, the owner started chasing after Tchale.
However, the convict stopped after running for a distance and the two started scrambling for the bag of maize. It was during the scramble that Tchale produced a knife and stabbed Jonasi seven times on the arm.
Tchale hails from Chipoka village in the area of Traditional Authority Kalumo in Ntchisi district.
Zitsiru tamasuren munthuyo chifukwa choti sanakupasen zammanja agalu mbunzi nawe mfana uyi sova kkkk uyisovenge
Nde mwamuna ameneyo
Si a chewa awa eeeee koma abale sisss
mwapanganji man muchingobwera kuno ku jons kuti mudzaone momwe anthu amasinthira moyo sudakadzabaso ee 10 years zizohezatu udzapeza ndiri ndi ana awiri ambwana
confused.-_”;)/?!,–__)/;:'”:?#*!!?? what’s wrong with this conviction
Mbava imeneyo ikhale kundende.
Wina Anaba Ma Million U R Saying 3 Yrs,woba Chimanga Cha Less Than K5oooo U R Saying 1oyrs. Amalawi
ameneyo apite basi
Everybody must type LEVITIKO 20:13 in support of Ken Msonda on gay
its jst started….killing wil follow…due to anger unless government must buy maize ans put it in admarcs
Mwammangilanji munthuyu?? Mlekeni nayenso ali ndufulu wokuba monganso ufulu alinawo ma gau.Milandu ya anthu okuba ndi ena okupha sikumveka mpaka pano zaka zikutha milandu ikadaweruzidwabe pomwe osaukafe kupalamula lero sikulomwero nkhani yaweruzidwa + chigamulo mkupelekedwa.IMFA YA MATAFALE+CHASOWA kwa mangidwa anga????? #MULUNGU adzaweruza inu oweruza dziwani
29 years plas 10 answ 39 eeee chizakhala chili ndi phavube chikazatuluka chizatibayasi
Thus too much, but neither the less perfect panishment must be giveb to him
Zachepa zakazo….. Kuba + Kufuna kupha guys tawerengerani bho bho munakakha inu, muziganiza b4 kuyankhula.
Anthu. Monga ma mp and president anthu amenewa amatiwotsa zinthu zoopla kwambiri akuziwa kuti Ku Malawi ntchito kulibe anthu ambiri adzikomo ndi osawuka akayitenga kuti k26000 ya fertilizer izi amatipanga chifukwa chokuti samatiwopa Koma I hop that people from Malawi will change our mind very soon tiyeni tikhale ngati anthu a ku south Africa ogwilitsana zochita boma likati no ife yes boma ikati yes ife no please guys
Very stupid, those cashgaters how many year r they get? 9 moths is enough
But gwaladi-raping case has died a natural death.
Do proper research on the law. The case is Robbery with Violence c/s 300 of the penal code. He deserves it.
Asa koma iwe
Eeeeeh tiziphanira njala yake yomwei? Kumubera ndikumubayanso?
John tembo atamupeza ndi mlandu wakupha agadama ndi zao adangoti apepense awa sangawauze kuti apepense koma zaka 10 kkk
Zigamulo zowona khope kusauka
who is a ntchisi magistrate guyz dis guy he doesn’t think whn he hand years to convicts why? koma asamayende kutali meneyu just send me his or her full name I will ssort this assholes for u pipo of ntchinsi infact of Malawi
Bcoz of Peter sakulabadila za anthu K26000 abag of fertilizer akwaniseyo ndibwana kukhapana kulipodiapa
Eish
“this hapened on 17 november this year” hahahahahahahaha malawi24 imeneyooo
wakula watha uziona akamati uziona sikuti amanena ndalamayi koma kuti mavuto ndiye usova
Chulungamo chabisala makobili nyimbo ya #NKASA oba nkhuku 10yrs wa cashgate 2yrs.
zaka zachuluka mulandu wakuba chimanga chomwe ndichakudya boma lili masomphenya pa anthu pls njala ndikanyama kena
Koma umphawi sikanthu inu kampeni kanuko 10yrs mukaseve anzanu amaombera mulandu wao umathera pa belo. Mmmm zakuvutani basi
Ayisova
Mmmm sidzinachuruke coz munthu yu wapezeka olakwa pa
milandu yiwiri; —
–Kuba katundu…
–Kuvulaza munthu ndi mpeni….
Aaaaaa,,,,akanaperekedwa mmanja mwa wanthu kale apange naye.
ziko la agalu ili oweluza milandu onse agalu.
10rys mphawi waba chmanga half thumba….3 rys wokuba mamillion end mpaka pano sanamangidwebe…
Pot ndi mphawi ten years koma mwana wa minister not gulty ,,,,,,,
Zakazo zachuluka zikadakhala zitatu bolani koma ten.majajinso mukuonjeza kwambiri mukuonangati zaka ten ndichibwana eti.
Bt cashgate Eliza tethani 3years only hence anthu ambiri akuvutikabe/kusowa mankhwala chifukwa cha cashgate
uyo 10 yrs ukuba chimanga, koma a cashgt, okuba ndalama zankhani nkhani ena mwa iwo mukumawapasa 2 yrs
Chocho ,amalawi osapanga zako bwanji,
AMPASA ZOCHEPA
Yaaa other one we can take lesson cause Malawi ndi dziko lantendere osat kubelana ngat pa SA ai
Wachibwana ameneyi amuchapenso makofi
With hard labour