Lhomwes snub Mutharika, demand their own country

Peter Mutharika

President Peter Mutharika migh soon need a visa to attend the annual Mulhakho wa Alhomwe festivities if the plans by people of his tribe come to materialise.

Media reports have said that a group of Lhomwes from Mulanje and Thyolo are demanding to have their own country following their dissatisfaction with the way the Mutharika regime is handling their grievances.

Peter Mutharika
Snubbed

According to the reports monitored by Malawi24, a group that calls itself People’s Land Organisation (PLO) has challenged that it will be seceding from Malawi to form an independent country come December 17 because of the failure by government to address their grievances.

The group which is operational in Mutharika’s home district of Thyolo and Mulanje has been demanding that the people of the districts get paid for the tea estates that are in the area.

It is said that in October this year, President Mutharika met with the leadership of the group as well as Parliamentarian and comedian Bon Winiko Kalindo who is also championing a similar cause in Mulanje district.

Reports suggested that at the meeting, Mutharika promised to look into their complaints but to date nothing has happened. This has prompted the group to think that seceding from Malawi is the only best choice they are left with.

The calls for secession of the Thyolo and Mulanje districts come hot on the heels of another group calling for the secession of the Northern part of Malawi owing to what they claimed was being left out of the country’s developmental agenda.

State house is yet to respond to the threats.

 

Advertisement

538 Comments

 1. Alomwe fuck u mulibe nzeru..inu zimenezo mukuzitenga kuti inu abuluzi??kadziko kanuko ndizabwera kuzakaphulitsa ndinyukiria mukapangire zimenezo kugraveyard zaucikapezo……..

 2. iiiii Nkhani sa minda kapena chani!!! pari ndale zoopsa zofunika nzeru za mulungu… nkhaniyi ndi phwake wa fedolizimu inayamba kumpoto ija,izi zikuchitikazi ndimadzi a faya fita kuzimitsa moto omwe unayamba kale kumpoto…khalani ochenjera musagone..

 3. ndiye mwati ikhala united states of thyolo ndi mulanje? kkkkkkkk president wake mkudzakhala Peter munthalika , vice born kalindo winiko ndi mphavu guys

 4. Nde zanyaupe zimenezo,, they don’t have any other way to follow? This z a stupid decision they must think as they r elders not babyz

 5. Alomwe simuziwa kulima zakudya zanu nokha ndiye munthamangise azungu mudya chiyani,chifukwa mumakonda ukalima fodya kukasungu ndiku mpoto Rumphi ndipo mumanyamula family yosi zisilu aLomwe yino

 6. Mukufuna malo olima yet ndalama zafertilizer mulibe mukudalira wa subsidy now ndalama yogulira fertilizer wa subsidy mukupeza mma estate aazunguwo now akalindo akukunamizani muvutike ndi inu asi ileni nkhaniyo okha mwapadela akalindo musati amalawi koma mufuna ndi inu musabisale kuwanthu

 7. Kanthu ako ndiye mwati united of what? Ha ha ha ha ha president munthalika wapengesa anthu misala Koma I don’t blame president but who voted for you kuti uononge dziko mumalo mokodza dzinthu uli busy pointing finger mImayi kapena anthu ena pena school imachita bwinoso and ukhalaso ndi nzeru za umunthu bwana president munaphunzila ma school akunja odula but zikuonesa ngati munaka mphunzila pa Thyolo cdss Koma night school

 8. Achewa kubeleka kwanu ndikochititsa manyazi azungu sangakukwaniseni tsiku lina azakunyanyalani.,, bwerani ndikubwerekeni scientfic calculator

 9. kuthamangisa azungu mudziko sizabwino mwawona chalu chathucho kuli umphawi chifukwa chothamangisa azungu zknthichito zikusowa tawanthu tikubwela kuno ku south africa chifukwa chosowa ntchitu mwawona mumene linathela ziko la zimbabwe chifukwa chothamangisa azungu ambiri akuzimbabwe aliso kuno ku south africa akugwirila azunguwo anawathamangisa kwawo kuno ku south africa kuli ulemelero chifukwa cha azungu akathamangisa azungu ziko lino la south africa lithaso ngati zimbabwe ,, please pakupanga zinthu aziganiza asathangise azungu mwina ziko lathu langapite pa sogolo tibweleko kuno ku dziko la eni ake

 10. Historically anthu onse aku Thyolo ndi Mulanje anangobwera mukafufuza ma T/A ambiri sikwao as of now mfumu ya chilomwe ndi imodzi ena onse ndiobwera so palibe chifukwa choti azivuta pano zamalo after all ambiri mwa iwo amakatengedwa maboma ena kudzagwila ntchito mminda ya tea. Living example ndi T/A Bvumbwe he is from Ngoni tribe so can he claim kuti azungu anamulanda malo amakolo ake..?

 11. Akalindo ndi winiko ameneyo nzake wamafumu matiki mzeru zake ndizopelewera,Akawone ku zimbabwe mmene athu akuvutikira kamba kothamangitsa azungu mkuwalanda malo,Iye mmesa waphunzilira ndalama za mu tea momwemo?Wazindikira liti izi?Akapitiliza amalawi 24 mundiuze mwamva??

 12. palibe adzalande minda ya anzungu amenewa bcoz ndi alease bola lanu la dpp lo silingaswe lamolo la land act.lease is 99 years. E ndye mungotha nthawi yanu.ndye enanu munalowerera lease yamwini ku central region coz of dem harsh regimes

 13. That decision is very stupid, they have a genuine argument but that is not a solution. They should find another way of solving the matter.

 14. Ngati mwasowa zolemba a Malawi 24 ingokhalani chete..osamalemba nkhani zopanda mutu!!kupenga kumeneko..ngati wina afuna Dziko lake apite ku Mozambique,akampeza Renamo alikonko ndi Gebuza…

 15. Kkkkkkk kma inu osamangodya Napwiliyo ndi makakawo bwanji kumeneko,mukakhuta nandolo bas.kungomva kut Bwampini akuchokera komweko bas

 16. Muhlako! Muhlako !Muhlako ! Ndakuitana kangati? Why do you want to fool this nation? Mwawona vuto lanu,we gave u an inch u want to cover a mile? Pliz Pliz I beg uyu musiyeni akupangatu sewero uyu.

 17. Mulanje ndi Thyolo likhale dziko palokha? kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk Ayi tionera iwo,maboma awiri apange dziko akatero awathamangitse adzungu, eyaaa hai mtokuonanitu

 18. chamba chimeneco iwe kalindo ukuyambisa ndiwe ngati zakuvuta pita ukapitilize zamasewelo zako zija manganya akudikila iwe ngati akukaya akulephela kuyambisa DRC chitumbuka iwe ndiwe ndaninso.

 19. Kod mbuzi zimemez bwanji, mukufuna tifanane ndi #zimbabwe et? Muganize bwino ndisanaku…….comment loading….. bysop zakumache….

 20. Why not give them their little kingdom and see what next. They will need funding to build their own iinfrastructure including issuing passports to cross into neighbouring Malawi. Malawi can introduce a Visa for them and charge them duty on their products which of course will need the trade routes in Malawi to get to the markets. So their economy will depend on Tea…The list goes on. They must be dreaming big time…

 21. Komandiye makape inu mwatha mawu bwanji ndine mlomwe koma ukamati mutenge mlomwe azikulamulilani pano akukulamulira nindani. Muzirankhula nkhani zoyenera kulankhula iwe ndiye wantundu utiuti ukati alomwe ndi mtumbuka ndiovuta

 22. MUSAYELEKEZE KULANDA MINDAYO.TANGOGWILIZANANI NDI AZUNGUWO AKUTULIRENI KWANUKO.AZUNGU NDI AMENE AKHALA AKUTUKULA MAYIKO AMBIRI MUNO MU AFRICA.TINACHITA KOIPA IFE AMALAWI KUWATHAMANGISA AZUNGUWA SIBWENZI MALAWI ALI CHONCHI.ANZATHU AMENE ANACHEDWELAPO MAIKO YAWO PANOPA NDIWOKONGOLA.IFE KUPUPULUMA.50 YRS FOR NOTHING.

 23. Bwanji alande kaye mulli malo amene wakhala akulanda anthu ku thyolo ndi kumulanjeko?maganizo opusa chifukwa sizopindulira anthu ovutika.

 24. Mwapanga bwanji anthu openga? muzagula nazo brouz kuyesa gwanda kamba kotengeka, wakuda akutsogolera maganizo opanda pakeyu anaphunzira nde poti nthawi zina ena sukulu imawapatsa uchitsiru coz I know these are not ideas of people from the grassroot ,we hv a university here lets promote the education sector so that our sons & daughters are raised in a way that they can positively face challenges in this modern world,the services that are derivered by these whites people cannot be done by us coz we are full of jealous & selfishness,Mtima wa thirani mwangamu basi,mubwereratu ku…….

 25. Nonse amene mukuika ndemanga zopusa ndinu makape, ndipo palibe chomwe mukuziwa! Ife tikufuna malo amakolo athu ndi cholowa chathu. Azungu wo kwao kulibe malo? Ife tizizunzika m dziko mwathu momwe? Malo athu atibwezere kaya titani nao ndi malo athu basi! Ndipo sitikubwerera mbuyo kaya tifa kaya atipha koma tifera malo athu. Kwa inu amene mukuti ndinu aku Thyolo koma mukuopa khalani koma malo athu atibwezere basi!

  1. Mufela zopusa…..don’t fight a loosing battle…just work hard in education and mubwele kutauni….azungu anabwela iwe usanabadwe ndiponso Manolo ako asanabadwe….akhoza kukhala ofila khungu koma Ali ma citizens of Malawi

  2. This is not a loosing battle my friend, we will win against these whitesettlers these are just citizens but we are the owners of this country and the land belongs to our forefathers. Mind you gyz we are not here against governiment, government is there just to asist us to bring our land. back.

  3. sometimes life is a cycle its good to learn from our friends mistake…(Zimbabwe) in case you have been given the chance to take over the land what will you do?? r u going to make farm produce the way these white men are producing?? secondly are you going to feed Malawi from that land the way white men are doing?? they way i see this issue is all about greedy, Jealous coz white men are developing , Leaving comfortable life while the owners of land are struggling …..God does not give equal resources , everyone is given resources differently just utilize the little resources you have well

  4. Decision of confiscating the land is agood idea,but the problem you are bringing this issue while Malawi is at a risk or at astake.Reserve this issue and bring it while Malawians are at a right angle.My Friend bear in mind that agood citizen right now is busy finding the solutions of dealing the economic hardships than so called problems in those two districts.

 26. Alomwe muziwona mwakula mwantha,padzana ndi uja mmati tivotere wakwathu lero ndi uyu wangoti phee without taking any action pamavuto anuwo!Next time tikamadzasakha atsogoreri lets chose patriotic ones osati poti ngwakwathu kapena ndimapemphera naye!!Finally,pepani kwambiri angulu koma ngati mukuganiza kuti moya pete alowerelapo apa nde iwalani!

 27. I didnt know we have such daft people where i come from. Fools for life. Yapping of farming when all you know is make babies,get drunk and get aids, lazy ass niggas that got no brains and proper mindsets, state nde zichani. When northerners did it they were stupid and yall sound way dumber and stupid by the minute. Could you build those factories if you had that land? And your weakasses wouldnt make tea part of what malawi depends on as the main export coz you lazy and you talking separating from malawi. Tell your PLO fools to go back to school and take the village farmers with them. #Demeti

 28. Ma Estate akunenedwawa atapatsidwa kwa anthu akuda they cannot manage them coz they dont have resources,azunguwa amaononga ndalama zambiri to manage them,go 2Mangochi anthu ena ammaboma awiriwa anapeza malo mu program yakuzigulira malo,ambiri anathawa kubwelera kwawo kamba ka ulesi ndi umphawi,azunguwansotu kuno ndikwawo,ambiri akhala kuno zaka zambirimbiri

  1. Who told you that they cant manage them? I stay in tea estates go and see black people are taking great positions which were held by whites and ukamati they dont have resources have you come accross the tea processing? Its all about machines which are purchased through south africa and its all about plucking,sorting,withering,drying,fermantation and putting it in a mortar and all these works are done by black people, Malawians as a mater of fact and ena mwaiwo got high positions than whites so ukutanthauzanji mfundo yakoyi? I dont agree with you,the issue is: they cant chase them not if they chase them who will manage the companies

  2. Chabwino ndi chan kut #Azunguwo aziwapezesa mway wa ntchito #Amalawi kapenanso kukweza ntchito zazokopa alendo ma #Maboma awiri amenewa kapena kuwapasa malo #Amalawi ndikukachosa tea yense, kudula mitengo yonse ndikumangako misasa mphepete mwa #Misewu ija ndikumangoberekana ngat #Nchenga ali pheeee!!! kom akulephela kupez chakudya, fertilez ndi ana umphaw wazawoneni chabwino ndichani……?

 29. The implication is.. Thyolo gets independent, Peter becomes a foreigner and gets out of power with immediate effect…….crazy. Malawi!! 🙂

 30. zomangowopa dona kodi dona tidzamuopa mpaka liti? we need our land, tikunyozeka ife moyendamu kuti kwathu kulibe minda yeti our land inapatsidwa kwa azungu. tikufuna minda yathu full stop.

 31. zomangowopa dona kodi dona tidzamuopa mpaka liti? we need our land, tikunyozeka ife moyendamu kuti kwathu kulibe minda yeti our land inapatsidwa kwa azungu. tikufuna minda yathu full stop.

 32. Nzungu ndi nzungu olo atakusiyirani malowo mindayo muifelexaxo mukhara muthengo paja mumakhara achangu pochita zinthu musiyen nzungu atukule kaye kumeneko asa united of thyolo n mulanje iti itixo imenei kungofuna kumupaxa president preasure .

 33. Ine ndiwa kuthyolo. Kumpoto akufuna dziko lawo, Mulanje ndi Thyolo nawo akutero. Ndikadakhala President ndikadawapasa go ahead. Azindikira liti kuti azungu adawalanda malo? Nanga ndi ma billions angati omwe boma limapindula kuzera mumisokho kwamakampaniwa? Nanga ndi angati adzazuzike azungu akathamangisidwa? Kusamvesesa ubwino wamakampaniwa ndizomwe zawapangisa ena kupanga timabungwe tawo ndicholinga chofuna ndalama basi.BOMA la Thyolo ndilotukuka kamba kamakampaniwa komaso magesi adafika kumizi kamba kamakampaniwa. Zipatala,masukulu,misika ndi mabwalo adzamasewero ndidzambiri kamba ka makampani. Ena ngati zaka zakuceperani sibwino kusokoneza miyoyo ya ena. Minda makolo athu adali nawo ndipo adatipasa koma kamba kosasamala ndikusalera minda idatha ina kuguga kamba kakusazindikira. Azunguwo amasamalira thats why ikuoneka bwino even atanyamuka lero ndikukusiyilani mindayo within two years muyisakaza ndikuyamba kutukwana boma.MY thyolo! My boma! GALAMUKANI

  1. Akulu mwalankhula m’zelu yabwino kwambiiiili, ndipo atat tisankhenso inu nde ndinu olowa lowa. Anthuwa mitu yao sikugwila angopezana odwala okha okha.

 34. Vuto si kalindo but ma brouse omwe amavala ndi amene amamupangisa,mukathamangisa azungu muzavutikaso plz akalindo think as aman not awoman

 35. Azungu Anapasidwa Malo Nthawi Ya MCP Not DPP coz Anaona Phindu Limene Mafactory Atea Angabwelese Ku Mw and nthawi imeneyo palibe akadandaula za malo coz chiwelengelo cha anthu chinali low koma pano zachisoni munthu wa zaka 18-20 koma ana atatu ,banja kungokhala la ana okhaokha ndye mukudana ndi makampani mukufuna azilemba anthu 8000 mmalo mwa anthu 4000.Nde tingopempha Makampaniwa Kut Azikhala Ndi Minda Ina Azilima Chimanga Mkumathilira monga Momwe Amapangira Tea Kut Azithandizako Boma Kukhala N’chakudya Chokwanira.

 36. govnmnt must nip it in the bud. muluzi wa galu ndiumozi Chikhwawa Nsanje, Dwangwa azafunanso zokhazokhazo ndiye lizakhala dziko?

 37. malaw ndi wamkulu osadana nd azungu ndamalawi nawoso,,inuyo denkhani yang’anirani bmalo basi koma azunguwo akupanga contribute ku dziko kuno than we black ppo,,koz mufuna malo mudzilima kenako mudzanenaso kut mufuna makoponi pamene azunguwo ayi.

 38. Akuona ngati dziko mchibwana,,patukana mwina Malawi izachoka pa#1 kufika pa#2 pandandanda wamaiko osauka,,dziko lanu lizakhala LOSAUKITSITSAAAA padziko lonse lapansi + dziko lonse lakumwamba,,,we wil never miss u,,,, ndiye mwati lizakhala dziko lanji??????? Flag???

 39. Zomvetsa Chison Amalawi Kumagotukwana Bas!Chonch Stngalandle Madalitso,guyz Chepetsan Kutukwana Pa Fb Plez Plez

 40. population ya anthu a thyolo ndi mulanje is ma native ai. tea ndamene anapangisa kuti chiwerengero cha anthu mmabomawa chichuluke, osati kuswana ai chiungamo chake nchakuti ambiri a ife pobwera tinapezamo kale azunguwa tea atayamba kumulima, tangotengerapo mwai chifukwa choti azunguwa sikwawo kuno. Nanga amang,aja ndi asena kuchikwawa plus dwangwa ayambenso kuvutisa za malo amene illovo ikulimapo sugarcane? because is the same situation. u r going to create another problem

 41. Sim’matonva inu eti? mumtenge m’bale wanu otha mano mkamwa akutisokonezela dziko lathuyu muzikakhala naye ku united states-ko km mukadasankhako dzina lina mpaka #united_states kkkkk kaya musovenge

 42. Eee nkhani ndiyoti iwo akupindula ndi malowa ndiye ngati dziko ndi ife eni nthaka ayenera azilemba antchito ambiri kuti nafe tizithandizika ngati dziko lathu.Koma ngati iwo akutenga malowa ngati awo ndiye kuti amalawi tiyenera kulanda kumene ngati dziko lathu. xenophobia

 43. yes let it be ngat kuthandizana pabanja kwakanika tikuyenera tigawane mapoto pokhapo mwina mungazindikire kut manyaka munasankha pachisankho chanu chija sanatisangalase thyolo ndi mulanje khalani panokha kumpoto nakonso khalani panokha zisankhiren yemwe angakuthandizeni otherwise tikusamira chodyedwa ndichiswe tigela limodzi

 44. Muziyenda kwao kwa azungu inu simungakhale ndi malo kuposa eni ake ndipo ndi atsankho chonde amalawi muzimverano chisoni anzanu akamadandaula, ndinkona muli osauka chifukwa chosazimenyera nkhondo koma tulo basi! Asieni akufuna chilungamo

  1. Akagawana malowo, akapitilira kuswana kwambiri kutsogoloku adzagawana malo andani? Nkhani ndikulimbikitsa kukhala ndi ana ochepa (3)

 45. #Kumayamika_Dr_Bakili_Muluzi, anamanga nseu wapamwanba kuposa nseu wina uliwonse M’malawi muno,,, ndipo ulibe chigamba #from_Blantyre_via_Thyolo_Mulanje_mloza boder. pano ukutha zaka pafupifupi 15.Osati zamisala zomwe akupanga a #Moter

 46. Anthu amene mukuti nthawi yonsei analikuti simumaganiza, kodi ngati chinthu chinalakwika sichikonzedwe? Nanga poti boma silikuwathandiza mukuti atani? Changamukani inu siziko la azungu Malawi kugona!

 47. Kumbukilani kuti zikoli lidali ndi anthu 14 milion panopa 15 million nde musalankhule motumbwa apa dziwani kuti Mulanje, Thyolo ndi chiladzulo ndimaboma amene anthu ake amasamusidwa pa program ya kudzigulira malo pamene kunena zoona mabomawa malo ndi ambilimbili koma kuti azunguwa adatenga malo ambili.

 48. Anthu akumulanje pitilizani coz sinthawi ya asamunda ino kuti tizipondelezedwa Amalawi coz cha asogoleri adyela ndi opusa ziko ndilathu ili ndipo magazi azachuchadi oneday!

 49. zikatheka mumutenge mlomwe nzanuyu azikulamulani. M’mene azungu amatenga malo inu munali kuti? osangopempha kuti mukufuna malo olima bwanji?? or atakupasani, mindayo inu mungalime chani??? Sikuti tikukukakamilani koma ndinu athu onvesa chison

 50. Anthu amenewatu apange dziko lawolo, akatero a tsogoleri onse nduna komanso prez azipta kudzko kwawoko, nanga tizizalamulilidwa nd anthu akunja ku USTM ngat kuno kolibe anthu?

 51. Azungu akunenedwawa anayamba kulima liti mindayi?Nde mukakhuta deya uko mkumazinamiza kuti mulande minda ati anakubelani,inu mulikut nthaw imenei? Pajatu kuchipatala amaphunzitsa njira zolera inu muli ayi mpaka ati ana athemo kkkkkkkk musova aphwanga ana enawo pinyolo basi

  1. U are very stupid mupite ku south africa anthu akufuna malo awo muziyankhula ngati muli ndinzimu population ikugwilizana bwa they have to refund the land they stolen from pple its not new story any country now is forcing these white pple to vacate

  2. Usalimbane ndi alomwe opusa ukhonza kukhala iwe they r fighting for their land if u have nothing to say be quite rather than kumayankhula zapamtumbo paamayi ako

  3. You are so goofy and so stupid,i can see you are just a male not a man kupusa ndipolankhula pomwe zoona? Nzeru zako nzoperewela eti? Wamatewe mkamwa iwe cant you see these white people are causing poverty by stealing and using our resources for their purposes? Ndiwe opusa and i can see you are not even a man

  4. Koma #Madalitso nd #Jordan basi inu mtima pansi programm ya kuzigulira malo ija akut iyambanso m’madera a Nsanje,Chikhwawa nd Chiladzuru.Mukalembetse changu.Sizotukwanazo apa ayi.

  5. The pipo myt hav sense but my questions are: where were they all this tym? Azunguwo azindikira lero kut akuwabera malo ao? Amadikira kut bon kalindo akhale kaye mp? Kodi akapanga ma district wo kukhala ndi dziko lao lao ndiye kut azunguwo achoka? Ma court ake omwe azipita kukasova nkhaniyi azikhala aku mulanje ndi thyolo? Akulephera kuchotsa azungu pano ndiye angakwanitse kuwachotsa when they form their so called soverign state? U may castigate pipo coz of their comments but u shud also question ur arguments coz they are the bone of contention. It was atumbuka at first pano alomwenso akufuna dziko lao lao kkkkkkkkkkk “malawi wa lero”

  6. Am also Lomwe nd currently am at Thyolo Boma.But sometimes i ask myself alot of questions why how what and where were these pple? When you criticise them they start insuliting as u have already seen.Now they saying they want to form their own Government and it will be Governed by Winiko,zachamba zenizeni.The same Winiko he was the one who led the pple in Mulanje district to open their new garden in Mulanje mountain.As of now mj mountain is now a desert.Ayi musalime muphirimu muwanva tikulozani but what you have to know is that you are creating your own problems and you will be the one who will suffer olt.Muphiri mufunse aliense amene amautsata ulimi simumalidwa mbewu, mitengo yokha basi. Nde tatukwananinso koma ichi nde chilingamo chake chabe kukuvutani kuvomeleza.

  7. Ok zikuonekakuti anthu ambiri ndinu mbuli pankhani imeneyi, Anthu sakufuna ma tea estate koma akufuna malo omwe ma estate samawagwirisa ntchito amangokhala kuti agawire kwa anthu kuti azilima, komanso ma tea estate asamalembe anthu mwa ganyu koma permanent kumawalipiranso bwino. Nde izi nzolakwika. In zimbabwe, south Africa even in kenya they did the same,nde kumenekonso ndi Alomwe amene anachitisa kuti polima pachepe malingana nkusalera kwawo? I dont think so, because I am avictim of the situation.

  8. #Davie pena pake sindikukumvetsa,ukuti anthu sakufuna ma tea estate koma malo omwe sakulimidwa.Nde malowo ndiandan? Komanso wat anthu asamagwire ntchito mwa ganyu koma permanent,kodi m’mene makampaniwa amayamba kugwila ntchito yawo anayamba ndi anthu ochuluka bwanji ndipo chiwerengero chaanthu mdziko muno chinali bwanji? INETU POKHAPA NDE MUTUKWANADI.ZONSEZI ZIKUBWELA CHIFUKWA TACHULUKANA MALO OLIMA TILIBE NDE MPAMENE TAGANIZIRA ZOLANDA MINDA YAMA ESTATEWO.Ndikut kulanda coz mmene azungu amabwela kuno kumazayamba kulima nonse mukut tikufuna malo athu kulibeko.Nde tie nazoni koma boma sililora zachibwanazo

  9. Inayamba nthawi ya Bakili mma 96 ndipo iye pofuna kuthana ndinkhani imeneyi anachita introduce kuzigulira mmalo. Ndipo anasamusa anthuena mmabowa awiliwa kumapitanao kumangochi ndi machinga, Bakili yemweyo analamulanso kuti malo ongokhala agawire anthu kuti azilima posimikiza izi Bakili analanda Makande estate yomwe inangokhala nkugaila anthu kwinako kusegula prison. Bakili atachoka, ma tea estate analandanso malo kwa anthu ja ati asamalime mphepete mwa tea ndipo anakazula mbeu zawanthu usiku.Muluzi had a solution for the problem koma ma estate ndiomwe sakufuna kuchita zomwe president Muluzi analamula.Now the current president doesnt know this bcoz he was not there thats why he is silent on this issue.

  10. Thats a big problem among pple nowdays,they pretend to know yet they dont know, what they have at hand is a propaganda information,and they dont need smone to feed them with right information.

  11. @ Dave, zikuoneka kuti anthu amangothamangira coment pamene maboma awiriwa sanafikeko. Makampaniwa ali ndi malo ambiri omwe salimidwa. Tsono anthu akupempha malo ngati amenewa osati zomwe munenazo ai.

 52. Kkkkkk koma anthu aku thyolo n mulanje ine ngati ndimkadziwa kuti ndiopusa chotchi shame on you…

 53. Kikikikiki very funny Bon kalindo i think nw he is getting mad and those ppl following him……. Malawi is too small wat about mulanje and thyolo……… My home is Mulanje T/A Nthiramanja bt wat is happening is nt gud who are those ppl dat even Government should pay attention to them ontop of dat do u thing government should be afraid of idiots……. There is many of problems to solve lyk financial crisis so who is bon kalindo to come up wth stupid issue lyk dis….? When you are doing things don’t come wth alie dat ppl from village de are crying, whr were they all along….? U want to tell me dat those white they jst coming jst before dats nonsense they mst shutup their mouth fotsk

 54. Eeeee apange mwina enafe ndikupeza kothawilako ku joni kwaopsa komaso boma la peter likukhala ngati simalawi mpaka kugulisa zipatala??

 55. Kikikikiki very funny Bon kalindo i think nw he is getting mad and those ppl following him……. Malawi is too small wat about mulanje and thyolo……… My home is Mulanje T/A Nthiramanja bt wat is happening is nt gud who are those ppl dat even Government should pay attention to them ontop of dat do u thing government should be afraid of idiots……. There is many of problems to solve lyk financial crisis so who is bon kalindo to come up wth stupid issue lyk dis….? When you are doing things don’t come wth alie dat ppl from village de are crying, whr were they all along….? U want to tell me dat those white they jst coming jst before dats nonsense they mst shutup their mouth fotsk

 56. vuto lalikulu ndakumvan ndiumbuli womwewo anthu 500 simunganene kut ndizolakwika mwachokela kut ife2 atichoselad teayu mukamat tikubelekana kwambili inu kut muzpeka makolo anu amatan ayelekeze akakamile tiwapanga za mwana wa zungu anafela ku phili uja mwina mwaiwala zausilu eet

 57. Amene asadayende akhoza kumati kudziko kulinji?Dziko la Zimbabwe lidasauka komanso anthu kuzunzika chiyambi chake chidali chimenechi,tsono pali anthu ena mudabadwa ankhanza mumakalasa moto kukalasulila amphawi zikavuta inu nkumathawila kunja sibwino choncho,,,,,,,,,,

 58. mukamashosha dazi lathu poti ndife amalawi opusa mumva kuwawa kapena tiziti simunamvepo za mangochi boko halam

 59. Kale bwanji simunkawafuna malowo? Mmaona ngati kuswana nchitukuko eti? Ma parasites inu palibenso chimene mmachita contribute ku dziko. Kuchulukana. Kwanuko kumene kwatibweretsera mabvuto mdziko muno mnapangisa kuti mbuzi yi. Ikhale president,mbuli ya chabechabe. Mkhaledi panokha. We will not miss you

 60. Anthuwa kunena chilungamo zangovuta. Ulamuliro wa Bingu kunali kuzigulira malo .kaya pano zilipati ndi aphwawowa? Nthawi yonseyi anangokhala chete analikuti. Thamangitsani Azunguwo muone mbwaza ngati kwa Mgabe kuzimbabwe. Pano Anzanu ku Zimbabwe ali ndi ma currency okwanira four , dollar ya USA yimalowa Rand, meticas, yimalowa ngakhale kwacha yanuyo yikugwira ntchito kumeneko kamba kazifukwa ngati zomwezo. Mwangosowa chochita mufuna muzunguze mutu peter eti? Poti ndi waku Thyolo konko athana nazo. Ndiye mwati UNITED STATES OF THYOLO AND MULANJE , KIKIKIKIKIKI, Ndiye united yanuyi muyiyendetsa bwanji poti malo olima mulibe , sono ngati malo olima mulibe it means chakudyanso mulibenso ndiye ziyenda bwanji zitsanakhute zili ndi njala. Zanu zimenezo zikakuvutani musalimbane ndi peterayu. Kuyamba nkosavuta koma kumaliza. Ine ndili cheteeeeeeeeeeeeeh ndingokuonelani zikatha mutiuza.

 61. U kno, penapake umunthu waperewerapo apa. If government chases these azungu, wil they manage these farms on their own? Wil they run such factories? Eg Small holder z there, bt ndangat amapindula nkumapeza zosowa zawo zonse? Che Winiko pena be a reasonable person, k?

 62. Vuto si inu Koma makolo anu sanaunikire chodza mawa, ngati kangakhare ka dziko ndiye kadziko kake kangakhare kotsalira komanso ka azimwale. Maloto a chumba amenewo chepesani ku belekana ngati mbewa .

 63. azungu sakuyenera kukhala ndi malo phwii pamene mwini dziko akusowa malo umenewu nde usamundawo. komanso naye mmalawi kumupatsa malo amenewo sikuti achitapo zanzeru ayi, atangolimapo mizele yake itatu basi, kenako nde aswana ngati ngumbi ndikumangamangapo tidzisakasa tawo. basi asapatsidwe malo amenewo asiyeni akhedawo akuchitapo zaphindu

  1. Don’t be silly. Its not fault of local people that they had their land grabed by foreign estate farmers so if u don’t know the truth behind the story is better to kip ur mouth shut. On whether we r overmuiltiplying or not is non of your bussiness.

  2. u havent understood a single pt pa zomwe ndalembazi. if u did grab a sense out of “zonse ndalembazo” rather than singling out some words, sukanakomenta s**t. i am minding my bznes coz malawi is my bznes. ur super silly than silly itself

 64. Amalawi mutamalembano nkhani zochitika enafe timafuna tizidziwa nkhani zadziko lathu ndiye mukumachulutsano kunama iwe amene walembankhani yakumulanje ndi kutyolowe ukunama unachokera ku motarara usipitse maboma akwathu uzitenge bwino wabva

 65. Zomwe mwayambazo mutipalamulira mdziko muno mavuto kuposa alipowa.Musayiwale kuti nkhani yothamangitsa azungu ndiyovuta.ku Zimbabwe zinatheka chifukwa ndi dziko loti muzambiri limadzidalira lokha.Mwaiwala kale za mzungu mmodzi tidamuthamangitsa uja? Please dont force the matters that are polical in nature inorder to gain your popularities.We Malawians we are not ready to do so because these will bring negative & bad images from donors

  1. ku Malawi tiliko 16, 000 000 akanati anthu 14,000 000 adziganiza chonchii NATO nyson table?????? aaaaa bwenzi tisalinso osaukaa….

  2. Ndie ukawapase malo akwanu azikalimapo. If I ask u simple question, can a Malawian own land in Europe? So should we lose our God given resources just because we are monetary poor? jack up!

  3. Ndie ukawapase malo akwanu azikalimapo. If I ask u simple question, can a Malawian own land in Europe? So should we lose our God given resources just because we are monetary poor? jack up!

  4. Kkkkkkkkkkkkkk akakupasa bwanji malo ku europe anga ulinchoti chikawapindulisenao atati akusiyireni ma estate omweo mukanikaso kupanga manage think kkkkkkkkk kungokusitirani zikhala ndalama zopezera akazi osati chitukuko #ndaseka

  5. Bwana Clemo,simunamvetse point yanga.I didnt say those people are having wrong ideas.Those two districts are part and parcels of Malawians people.Even the President himself can not buy the decision of confiscating land from Europeans now due to other constraints that the country is facing now.Mulanje and Thyolo being part of Malawian country there is aneed of properconsultations from Malawians citizens as awhole.Bear in mind this is a serious issue to All Malawians not only the peoples around those district.Together we can tie up a lion

  6. I want to asure some of you.Bear in mind we are talking about Estates not the gardens.Its only 11 countries in the whole world that are still prospering without investors from other countries.Remember symbiosis is not happening on rocks but on living things which people are inclusive.

 66. umeneo nde mukava kut umburi ndiumene muchitao atolakhani amalawi 24 be lyk u dd ua academic of dc work nat lyk survage pipo hw cn 1 coutry shared wt white pipo ??utsogoleri wanu ukulephereka2 apa evin president achitapo chan tizangozot malawi mwatigulisa tonse kwasalaku zimenezi

 67. SI ZOONA AYI COZ ZIDZETSA MPUNGWEPUNGWE MU DZIKO LATHU LINO.NDIYE KUTI ADZIIIMIRA CHILICHONSE PAOKHA?CHACHIKULU NDI KUPANGA ZA SIR ROBERT MUGABE KU ZIMBABWE,THIS IS OUR LAND & WE HAVE ALL THE RIGHTS TO OWN IT.AWAPATSE ANTHU POLIMA BASI.

 68. Kod mesa Bon kalindo wasutsa zmenez, nde mukunenazo nd ziti? Atolankhani a jce certificate kkkkkkkkkkkkkkkkkk, mpaka lero smukuziwa amene akunena izi?

 69. Welcome to Illuminati Temple India
  Are you business man/woman, politician, musician, soccer player or student and you want to be rich, powerful and be famous in life. Come be a member of the Illuminati Brotherhood and Achieve your Dreams…Contact us [email protected] now.

 70. M24, Ngati Nzoterodi Ndiye Kuti Bwampini Apitenso Ku Kadziko Kawoko. Very Tired Of This Old Styled Ndataboy. Ifenso Tichite Zathu Pano Pa CENTRAL. NB: IF THIS IZ MERE PROPAGANDA THEN “SHAME ON U M24” Iwill Investigate & Then Delete U Permanently On Internet

 71. I am so happy that i have to tell the whole world how i was cured from HIV.I never knew there was a cure till i came across a story of how a lady was cured of HIV by an herbal doctor called dr.IKUKU.I have been living a hopeless like since i tested positive.I contacted him and started taking his herb.Exactly 3 weeks he told me to go for a check up,i went and was confirm negative.It was shocking to me till series other tests still prove that i was negative.Till today i am still negative.All thanks to dr IKUKU.You can contact him if you have any troubling sickness.
  2348079062707 (whatsapp) or email:[email protected]
  This is real,he cured me and can still cure you.

 72. Pezani njila yothetsera umphawi musapeze njila yophwasula Malawi kuti anthu aziphana ngati nkhuku za kanyenya chifukwa chogawana ka dziko kakang’ono ngati ako
  Adm ngati ukulemba za boza uzasowa tsiku lina otsawonetse kuti ukuchenjera
  Upita kwa dyerankoko mountain ku Mulanje

 73. Hahaha this is foolish
  Chiyambi chakugawanika amalawi ….kodi Pitala okhala Lawyer sakuziwa zomwe zinachitika/zikuchitika ku Kenya pakugawanika kwa mitundu?

 74. Ena muli busy kutukwana Malawi24 chonsecho mumadalira yomweyo kut mudziwe zochitika mdziko lanu.More fire Malawi 24 enawa ndi msanje chabe chifukwa sadziwa kupeza ndi kulemba nkhani.Ine ndili nawe nganganga kuwerenga nkhani zako zoonazi.Enanu mudazolowera nkhani zabodza …

  1. Amai bwerani mudzalowe ku ndende ndi cashgate yanu ija,mbuli zophunzira sizikudziwa chomwe chikusautsa a malawi

 75. I am a bonafide Lhomwe, where are you getting this nonsense? Why do you write stupid articles aimed at dividing the nation? The editor of this page is a big fool and a shame.

 76. I can’t wait to see the lhomwe government. ..
  Ndiye kuti munthu akuyenela kudzakhala ndi ma passport awiri.
  Ya ku malawi ndi ya ku mulanje .

 77. These people are mad they must come up to their senses Lhomwe people they must know that Malawi its not their own in fact they must coil we will not let that barbaric act to prevail in Malawi

 78. ineyo chinthu cimodz comwe cimandipweteka ndico kunyoza malawi24 ngat yaupandu kod iwowa angamaike unverified news?ngat ndiconcho amangitsen cifukwa lamulo lilipo ndipo ineyo kut ndiyambe kulitsatira dzikoli ndi malawi24 yomwei inu mukunyoza, abale anga bwanji kod ngat zakukhudzan ingosinthani zichitiro zanu cifukwa malawi24 just publishes what has hapened 4 malawians lyk u n me 2 get t samanyoza munthu ai musakhale inu iwo ali ngat maradio stations osiyanasiyana aja u know?

 79. foolish media. …. instead of writing about the solutions to the problems this country is facing, ur busy writing negative n false stories contributing to the already existing problems. … ..What is ur role as a Malawian. ..??

  1. Iwe nde mbuzi yamunthu, unazolowera kumva zaboza basi. Ine ndimlomwe ndipo nkhaniyi ndiyoona fufuza upeza bwamnoni iwe

 80. kkkkkkkkkkkkkk hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahah kkkkkkkkkkkk ,nde mmalawi mutuluka maiko angati ? nanga anzathu kuntundako nde nawo angainve kkkkkkkk

 81. It’s not a crime to reclaim your motherland only if you are willing to welcome back your citizenry in diaspora (Lilongwe, Blantyre, Zomba

 82. Kkkkkiest. Kkk ndiye mwati alhomwe? Akuti dziko lawo? Tsono amene akuyankhulawa anapeza malo ku Ma district ena ndiye atan? Koma dzina la dziko lawo likhala chani? Mmmh tsono pokambilanapo amasankhaso? Nanga bwanj ena sakuzidziwa? Koma mwati alhomwe basi, nanga ochewa, ayao, {atumbuka paja adayambaso}, asena, atonga, ndi enawa atani? Koma Malawi akatelo akhala dziko kapena mudzi?. INU MR 24, MULI SERIOUS KAPENA MUMAFUNA TISEKEKO? , Ooh ndikukanika kuzitolela izi, mulembenso koma zomveka bwino mwina mayankho ndingawapeze. NANGA CHONCHI ANTHU AYAMBA KUNYOZA MALAWI WABWINO UJA. Mmh anywy let me continue kkkkkkiest kkk

 83. Malawi is now becoming desolet…and desperate….every leader is continously subjecting the poor Malawians to the harshest treatment ever without any consideration.. As i say…Malawi……we are the only real altenative government in this country. Let us get united, we cannot allow efforts of individuals distabilise our nation’s unity…

 84. No my people..!! The solution is not to form your own government or country. We are the altenative government of this country. Let us just come together and fight for our children from these clueless and careless leaders. Why do we not enjoy the very democracy that we voted for in this land?

 85. Poti they av mentioned alhomwe u say kt Malawi 24 ndi yaboza had it been analemba kt atumbuka none of u wud av said that bt kuwanyoza n giving credit 2 malawi 24 mmmmm this malawi eish

 86. dziko lathu silingatukuke chifukwa cha anthu opusangati inu mumalemba khan zaboza just to win our attection.pano anthu ali kalikiliki kugwirana manja mtundu ndi mtundu wina mkumakambaso zopusa zake kayakumakhara kusowa zochita kaya.dnt u av life out side FB an Malawi 24?kupusa kaya mukumatumidwa kuti musokoneze but remember dis not all Malawians are Stupid as u think

 87. Akamati pali dziko lopusa pa dziko lonse ndi la Malawi anthu ake opanda mzeru koma ali ndi ma degree chomwe chikuyambisa mavuto mwa chiiwala kupusa

 88. Dziko lino ngati maudani akuchuluka ndichifukwa cha atolankhani. Thats why access to information bill ija ikuvuta.Kungoti ya passa imene ija azakhala mavuto. Azizachita kutiuza mpaka zoti mutharika lero walowa mutoilet kanayi. Atolankhani akumalawi akusoweka upangiri.

 89. wapeka nkhani iwe ndiwe chitsiru ngati wasowa cholemba kumangozikanda ku maliseche kwakoko, anthu aku mulanje ndi thyolo ake ati? patu pako wamva!!

 90. wapeka nkhani iwe ndiwe chitsiru ngati wasowa cholemba kumangozikanda ku maliseche kwakoko, anthu aku mulanje ndi thyolo ake ati? patu pako wamva!!

 91. Malawi24, why are you misleading us here. Do you mean if pple of Thyola and Mulanje form their own nation we will still be ruled by peter mutharika, why? Why wud we allow a foreigner to lead us. If they create their own country peter mutharika will go with them and will be coming to malawi upon invitation by our president to be, or when we are hosting Sadc and comesa meetings.

 92. Malawi24, why are you misleading us here. Do you mean if pple of Thyola and Mulanje form their own nation we will still be ruled by peter mutharika, why? Why wud we allow a foreigner to lead us. If they create their own country peter mutharika will go with them and will be coming to malawi upon invitation by our president to be, or when we are hosting Sadc and comesa meetings.

 93. Malawi24, why are you misleading us here. Do you mean if pple of Thyola and Mulanje form their own nation we will still be ruled by peter mutharika, why? Why wud we allow a foreigner to lead us. If they create their own country peter mutharika will go with them and will be coming to malawi upon invitation by our president to be, or when we are hosting Sadc and comesa meetings.

 94. Ndidzowonadi koma alhomwe mwataya khalidwe metsa munthu mudamupasa nokha mavote…okay fedal z gud deal…

 95. Kkkkkkk hahahaha nophiya ntundu wanga ochangamuka masewera pambuyo ife aromwe tikanena tanena sitimaopa kwathu njala imeneyi anthu azikalima kuti? Ndiangati amapindura ndi tea(masamba opanda ma vitamin wo)

 96. Malawi24, mwadya zambiri. Apa pokha nanenso ndiyenera kuperekapo maganizo anga. Apapo mwanyambita za m’manja. Kodi Mlomwe mumamudziwa? I mean do you know Lhomwes from Namamlha-Chidzadzulu, Mauzi – Chiringa , Phaloni, Chinani, Nambazo, (Phalombe)and those from the other areas of the remaining districts of Mulanje and Thyolo. May I call upon malawi24 to be objective in their reporting because from the statistics that I have from my research I conducted from 4th to 9th June, it is Peter, Peter and Peter. Sindikukamba za DPP ayi. Koma ndikuti come 2015, it is Peter, Peter and Peter and let me inform you malawi24 that Lhomwe Belt is a no-going zone for other parties and mark my words. Chakwera has no place in Malawi politics because he deserted the AG flock. Let me stop here as of now!

 97. The one who started to say that it menz is not amalawian.remember kamuzu said .it doent mutter which district you come from but you are amalawian is it true or …….?

 98. Malawi 24 bwanji mumafuna muzitukwanisa anthu osalakwa kumalembela nkhan zopeka,inu ndi amene mukuonjezelesa udan mziko,malo molemba zoona koma busy kupeka nkhan choncho dziko lingapite pasogolo? kenako tikupangan elminate bcoz we tired

 99. Kodi mumasowa chonena pa fb?mukufuna muzingowanamiza anthu kenaka ena otengeka okhuta mwano apezelepo mwai wonyoza HIS EXLLENCE NGWAZI PROFFESOR ARTHER PETER MUTHALIKA.President wathu wa dziko la mkaka ndi uchi.

 100. mukamalemba zinazi mudzauza argument zoona. ! muziwauza anthu zangozi zamb krismas za mpira zamb ndale osati zaboza. zanu wina amatipasa khani zochitika HAPPENED IN MALAWI

 101. mmm alomwe ake ati ine ndi mulomwe weni wen wakumulanje zabodza zimenezo basi ukangoona mulomwe wokhuta kachasu akulankhula zimenezi nde kuti alomwe tonse tili chomwechi kambani zina musatinamizile ife ndi alomwe takukanila ulembe zokhudza atumbuka! kut akutero mwina osat ife

 102. hahahahahahahahahahahahahaahahahahaha!!!!!!……hihihihihihihihihih.. !!!!!!!! hohohohohohohohohohohohoho…!!!!!!!!! hehehehehehehehehehehehehehehehehehehe*(*!!!!ahaahahahahahahahahahahahahahahahaha !!!!!!!! what a nice joke to end my day!!!!!!

  1. ooh!! people are not being serious. anyway that is another way of confirming that northeners are correçt on the idea of federalism

 103. zisilu nose amene mukukamba zophusa,mumaliziwa boma inu,kapena maloto?ngati dziko lonse lamalawi likuvutika pankhani yachuma,ena opanda nzeru akulankhula zopusa.ukuwona ngati mulanje ndi Tyolo ukuwona ngati angapange dziko? kuchulukana kwa alomwe kusakunamize wawa akumudzi.olembawe naweso ukule ungatukwanise anthu osalakwa.

 104. We do appreciate your comments. It let us know that some people believe Every Story they hear, without verifying if it is true or not..
  But Most of all.
  It lets us know that we do have idiots among us still.

  1. hahahaha, nice 1 Zagwa zatha tell them the truth inenso I just realised how ignorant these people are.

  2. hahahaha, nice 1 Zagwa zatha tell them the truth inenso I just realised how ignorant these people are.

  3. hahahaha, nice 1 Zagwa zatha tell them the truth inenso I just realised how ignorant these people are.

  4. hahahaha, nice 1 Zagwa zatha tell them the truth inenso I just realised how ignorant these people are.

 105. Musamawanamidzie anthu ine kwathu nku Thyolo T/A Kapichi koma nkhani imeneyi ndikumvera iwe, Kodi muzasiya liti kuwaudza anthu zabodza???

 106. kkkkk vuto la aphwitikizi akakhuta nandolo kuzikonda too much safuna kumvera za wina ayi. zili kumeneko kwa the republic of lomwe phwitikizi.!! welcome to phwitikizi government

 107. Zimenezi ndi zonama kwambiri, ine ndine mzika yeniyeni ya ku Thyolo koma sindinamvepo kuti boma la Thyolo ndi Mulanje kukhala dziko loima paokha. Tiyeni tiwauze a Malawi zoona. Zamkutu eti

  1. You are the same Lhomwes who make noise when the people of the north call for federalism. This is a fact and it’s on nyasatimes as well including other dailies.

 108. BEHOLD! I WILL SEND MY MESSENGER HOW WILL DIVID YOUR COUNTRY. LOMWE CAN’T WORSHIP YOUR IMAGE AS THEIR GOD! THEN WHAT ABOUT CHEWA AND CENTRAL REGION! AND NORTHERN REGION WATCH!!!!!!!!!!!!! POMPANO ANKHALA PULEZINENTI WA DPP BUT WITHOUT COUNTRY!!!

 109. Those of us who listened to the interview on BBC with APM the president DENIED any knowledge about this issue.Anyway tingodikira dziko latsopanolo kuti tikakhale nawo

 110. the Lhomwes havnt learnt that they cant make it on their own and that voting smbdy jst cause he/she is frm their tribe wont help and stll want their own country yet the whole south is being occupied by tea estates,bunch of idiots.

  1. Atumbuka mukuyankhula mwano koma chonsecho munathawa kutchire kumapiri kwanu kuja nkumakhala kwa alomwe omwewo. Enanu munali a kuda ngati kobibila kwa nyani. Panopo mmene munayamba kukhala kwa alomwe mwayamba kuyererapo pang’ono.Ndiye muyambe mwano lero?

Comments are closed.