
Amayi akhale patsogolo kupemphelera dziko, zisankho – Kwelepeta
Phungu wa dela la Zomba Malosa, Grace Kwelepeta walimbikitsa amayi kuti akhale patsogolo kuyamika komanso kupemphelera dziko maka pamene dziko la Malawi likuyandikira kupita ku masankho ponena kuti mapemphelo ndi omwe amabweletsa umodzi ndi kupeleka… ...