Atsogoleri tiwaikize m’mapephero pa tchimo la dyera – Usi
Wachiwiri kwa mtsogoleri was dziko lino a Micheal Usi ati mipingo ikuyenelera osalema kupemphelera atsogoleri komanso ndi adindo onse kuti asamatengeke ndi zinthu kuyiwala chomwe analumbira kuti adzachitira anthu uku atagwira baibulo kapena Quran. A… ...