Wamisala adawona nkhondo: kapena JB ankanena zoona? Anthu akufusana za Onesimus
M’modzi mwa oyimba odziwika bwino m’dziko muno, Onesimus, wadzetsa manong'onong'o m’masamba a nchezo kaamba ka zovala zomwe anavala komaso kupezeka kwake ku phwando lomwe anakonza ndi yemwe amadziwika ndi za ‘umgochana', Somizi. Somizi Mhlongo wa… ...