![Simplex Chithyola banda](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/04/Chithyola-235x176.webp)
Msonkhano waukulu wa MCP: Zikhale, Chithyola amwaza K76.5 miliyoni pogula mavoti
Sin’dazione adachezera kuziona! 2025 akusunthira chifupi, a Malawi yembekezani kuona malodza: Pomwe inu mukusowa ka K500 kogulira mchere, nduna zanu ziwiri zagula mavoti a ku konveshoni ya MCP ndi K76.5 miliyoni. Kuli kanthu kokanthula nchala,… ...