Wilson Banda is the governor of the Reserve Bank of Malawi which is the central bank in Malawi

Kwacha yagwa mphamvu

Anthu m’dziko muno akuyenera kuvala dzilimbe kamba koti pali chiopsezo choti katundu wambiri atha kukwera mitengo kutsatira kuchepa mphamvu kwa ndalama ya kwacha ya dziko lino kuyelekeza ndi ndalama ya dollar ya ku America. Lachinayi… ...