Reserve Bank of Malawi

Kwacha yada

Kwacha aithyola kholingo, aikang’antha, aichotsa chimbenene, aikong’ontha, aichosa mphamvu. Banki yaikulu ya Reserve yanena lero kuti yachepetsa mphamvu ndalama ya Kwacha ndi ma pelesenti 25. Izi zikutanthauza kuti wani dollar ya ku America yomwe lero… ...