Wanjatidwa kaamba kogwililira mwana wake yemwe ndikumpatsa pathupi
Bambo wina wa zaka 32 zakubadwa akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Monkey-Bay m'boma la Mangochi kaamba komuganizira kuti wakhala akugwililira mwana wake wa zaka 12 mpaka kufika pomupatsa mimba. Alice Sichali yemwe ndi mneneri pa… ...