Katangale wachuluka ku nthambi yogura ndi kugulitsa katundu wa boma – Cdedi
Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lati m’chitidwe wakatangale ku nthambi yogura ndi kugulitsa katundu wa boma ya Public and Disposal of Assets Authority (PPDA) wamanga nthenje ndipo Boma likuyenera kuwunika… ...