Zitayeni a Peter
Ikuvuta kuijama iyiyi. Akanakhala a Chilima mwina akanatimasula kuti paja akakhala pa mkhate si umo avutila kupha. A Malawi ochuluka ati Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika atule pansi udindo wawo ndipo afufuzidwe. Pa… ...