A Mutharika agula galimoto ya mamiliyoni ambirimbiri pamene a Malawi akuvutika ndi njala ndi kugona mu m’dima
Panthawi imene a Malawi ali pa mavuto a njala komanso kugona mu mdima, mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika azigulila okha galimoto yatsopano imene ikukwana ndalama zankhaninkhani. Malingana ndi ma lipoti amene talandila a… ...