DPP on Chakwera’s neck: he should be ready to leave politics and become a Prophet

peter-mutharika

President Peter Mutharika’s main duty in Mulanje on Monday was to launch the Likhubula water project but the Malawi leader and his ruling Democratic Progressive Party (DPP) underlings used the event to castigate leader of opposition Lazarus Chakwera.

DPP through its officials took to the podium to attack Chakwera for his opinions on the socio-economic hardships that have marred the country.

peter-mutharika
Mutharika’s DPP is not done with Chakwera.

The party’s Regional governor for the South Charles Mchacha told the masses that gathered in faith to witness the launch of the multibillion kwacha water project that he is protecting the party and Mutharika by castigating the leader of opposition.

“Asiye chipongwe chifukwa ife tikayamba kuyankhula nawo sizikhala bwino, akonzeke abusa a Chakwera kubwerera ku church 2019 (He should stop insulting us because when we start revenging things won’t be good, Chakwera should be ready to go back to his pastoral work in 2019).

“Sikutiso akakhala m’busa wamba akakhala prophet kuti azikazutsa anthu akufa ndi wodwalika (and he will not just be a pastor but a prophet so that he can be performing miracles),” said Mchacha.

DPP secretary general Ecklen Kudontoni then mocked Chakwera for speaking against Mutharika’s decision to hike the price of staple grains in Admarc depots.

Vice president for the party in southern region George Chaponda who is also minister responsible for water and irrigation also took time to dress down the Malawi Congress Party (MCP) leader before leaving the podium for Mutharika.

The Malawi leader began his speech by thanking the Mulanje residents for voting him into power in the 2014 presidential elections.

“Munandipasa ma voti 175,274 pamene a Chakwera munawapatsa 3000 votes. Yanga 82 percent, 18 percent yomwe inavotera a Chakwera kaya inali yoledzera but am sure sazavotatso (I amassed 175,274 votes from this area while Chakwera got 3000 votes. My votes represented 82 percent of total votes, the 18 percent that voted for Chakwera were possibly people who were drunk but am sure they are not going to vote for him again),” said Mutharika.

The DPP officials have since hit back at critics on the hardships the country is facing saying Mutharika is not responsible for the challenges but he is committed to find solutions.

Advertisement

311 Comments

 1. That’s the problem with this stupid idiot! Instead of solving the problems the country is facing he is busy insulting others ndiye tikamanena kuti alibe nzeru muziti timadana naye,

 2. Leav Dr Chakwela to rule our beloved Malawi frm,2019.after all your Government has shown alot of hicaps n potholes,hw long shld we b treatd wth un Godly,stupd n unfamiliar politics of Kaliat n others,they are the ones who’r leting Malawi to fail.Italk to u Pitala, to rule the country need someone to be lead by the Holly Spirit,n not being aprofesser wthout being led by Holly Spirit.Chakwela has been chosen by God to rescue the drauning nation.ur brothr failed the nation as well in the sense that he stipulated n escaleting on those who are said to be the big fish of cashgate.Its evidentedly that ur minstry iz also confined wth cashgate,why ur failing to prosecuit those who’r concerned wth it?Chakwela we’r waitn u triamphantry in 2019,cause we’r tired of these stupd mouse n choacoloches who plunders our Resouces n Revenues…..w’re askn God to hear our plea n wipe our teers…Noel Chiumia, Gauteng S.A.

 3. Mr Mutharika is not sleeping coz of Big man Chakwera……

  Why don’t you make your campaign by fulfilling your promises ?

  Simunapangepo or chimodzi chiloweleni m’boma but you’re still campaigning what a shame…..

  Munalowa mpaka muzatuluke mukupanga campaign ( non stop campaign) ?

  Ndiye anthu ena atulo kumawombera mmanja zafodyazi….

  Why akulimbana ndi Chakwera mkusiya unsolved problems behind?

  Wake up Malawi

 4. hahahahaha mwati chakwera atani,,,,,,,,,???? kmad aenera kukakhala prophet osat president enanu kaya mukulumkzana nd za odd version pano nd nthawi ya #JESUS tyeni tmulemekeze mbuyeyo osat politics….may b we love money thusy tikuthawako,,,,,

 5. Koma abale ndi alongo ndavesera ma comment ambiri onyoza otukwana osinjilila kulemala kwa dzanja kod akat anthu andale akutanthauza chiyan enanu ndinu ophunzila kwambili tien tisaiware kut ukuchokera kwathukuno kufikaso mapeto adzikoli kod alipo pleasdent amanena zabwino za otsitsa boma kapena otsitsa kukamba zabwino za olamula chot tidziwe utsogoreri atasankha ndimungu osat ifeyo yokha AI ndipo kunali zipan zambili zomwe mumazifunazo komazinarephera wanuyo amene mumafunayo mulungu akat yes adzawina koma akat no or mutamukonda bwanji ndithu muzakumudwa azaluzsso tiyen 2019 tion kut mulungu wasankha ndan koma zonyoza matenda sindikudziwa sanachite kufuna ngakhare achakweraoso athaso kudzadwara pakut iwoso mdimunthu ,,,,????

 6. Imene mukuti democracy inabwera ndi mipingo ku malawi, pangani chabe chitukuko choti adzakukumbukireni nacho osati ma launching …mpaka 5yrs

 7. mm instead of reflecting on the poor results in the just ended by elections! kodi bwanji ophunzilawa akupanga behave ngati mbuli! akanakhala a chair bwenzi choyamba akanathokoza Dr Chakwela for winning mchinji by elaction

 8. Zisankho za Unofficial kkkkkk ine ndiye sindidya ndale kaya!!!!!

 9. Athu amabuku sangavotele mbuzi za DPP ayi, bwina iweyo ndi amene ukawavotere popeza ndiwe mbuzinso, dnt you see all these problems, in 1994 one dollar was equivalent to four kwacha, but now one US$ is equivalent to MK725 , is this agovernment? What kind of the government is this if i may ask.

 10. Mmmm! Idoubt If Mcp Can Rule Again This Country, Unless If Chakwera Formed Anew Party Maybe This Coming 2019 He Can Have Avictory But Without Doing That He Is Just Wasting His Time.

 11. The poor Malawians apa amawombera mmanja ndithu posawona uphawi umene uli mmakomo mwawo. Amalawi tiyeni tisiye kuwombera mmanja zopusa ngati izi.

 12. mcp,chakwela kaya chatsika!,u are just nothing! make noise but you will never prosper. malawi singapange mistake yoika inu pampando.wat we r fighting for is gettin rid of u as main oposition party!! ufune usafune

  1. Iwe ndiye mbuzi yamano kunsi,citsiru,kape wama kape,mbalame,kafucheche komamso,galu wopanda nchira!!zoona umalikonda dzikolathu,kapena ndiwe youth cadet wa Dpp??ndizakugenda ndi marovu 1 day!Chakwela qualifies n deserve to b apresident in 2019.ndayankulaso cizungu siungamveso mbewaiwe????Viva Cakwela.casala ndikudula zanja lambuyewakoyo sopano tione agaru inuu!……asaah!undipeze pa web iyi:www.Noel Chiumia.Vivo.com gauteng johansberge OR TAMBO,Kempton park.

  2. kkkk halo sir,if i was a savage i could ve answered u the way u ve replied to my status but we must be different i guess. plus never coment my post at night just as u did. am not a watchman thak i must be awake midnights!..

 13. Even a Prophet can be a politician, he can change this nation to be the better nation through his wisdom given by God, since your level of education has failed to develop this country, so even U APM u can leave politics and let that Prophet takeover and see the wisdom of God solve our problems through that leadership of a Prophet!

 14. Even he himself APM should also leave politics and become a lecture of law at Chanco. Running the nation isn’t as easy as you thought in that time of JB, and now iam not ashame to say that JB was much better than you!

 15. Even he himself APM should also leave politics and become a lecture of law at Chanco. Running the nation isn’t as easy as you thought in that time of JB, and now iam not ashame to say that JB was much better than you!

 16. From My Assumption, Its A Clear Dethronement For The Whole Mcp Leader Trashing God’s Call Joining Political Dead Game.Does It Mean That Chakwera’s Spiritual Abilities Were Not Appreciated By God Hence The Diversion ? Our Mcp Leader Should Think Twice And Make A U Turn Before God’s Door Is Shut.

  1. Does It Mean That This Is God’s Call For Chakwera? By Looking At What Has Happened With Our Three Previous Presidents Its An Astray Route For Chakwera Since History Repeats Itself

 17. I was just reading all the comments but I found that bwampini Mr ibu pitala Malawians has lost faith in u with ur empty promises, Dpp has failed us ,so Malawians want to try the pres whe fears GOD ,I cnt want 4 the 2019 to vote for honourable Dr chakwera

 18. Kodi amalawi timaiwala bwanji kod si mcp imazunza anthu muno mayufi kugwilila azimayi anthu osalakwa kuphedwa kumakako amboni kuthamangisidwa amatengedwa mkazipakhomo mokakamizidwa kukagona ku elio ukapanda kupita kusonkhano ati wanyoza mfumu palinkhaza zambili mcp idachita kodi ambili amene mukuti mcp boma kapena munali muli ananthawi imeneyo akangoti lelo kuli msonkhano mawizulo mudzi wonse wopanda kupita amakwapulidwa ndiye mukamati mcp ibwelele aaa ndakaika mwina tisankhe china chipani

  1. Up to now some people don’t know the difference btwn MCP and one party system, that’s why DPP is closing down colleges to take advantage of such ignorant Malawians

 19. masiku ano mbava zikuyambila ku mpingo tisanamizanepo apa nde a lazalo olo atati ndi a prezdent azababe bas apa asamaoneke ngat iwowo nde abwino ndipo chot mudZiwe chakwera 2019 sakudzatenga boma adzathawaso ndi manyaz ngat ajawa atchona aja

 20. Dzanja likamulembere Chakwera zoona munthu amaneyu angasiye ubusa mkukayamba ndale mkumati dzanja lamulembera musamachite maseweratu ndi mulungu mukawerenge nkhani ya Yona

 21. If evryone is stupid then who is good? nkhani yonse yalembedwa munkhaniyi komanso macomment onse aperekedwa mnkhaniyi sikusonyedzerathu kuti malawi ndi dziko loyima palokha, tilibe president ndilibe anything zotiyeneleza kuti tili tsogoleri cause munthu ndi munthu nzache akulimbana” mukulimbana chani? palibe koma ndimphamvu ya satana dyelekezi

 22. kodi chakwera akadzuka mkuyahulira anthu omwe akuvutika zedi mdziko muno ndiye kuti walakwa?pali ma miliyoni ya anthu omwe akuvuti omweso sangatheso kuyahula kapena kudzudzula ndiye owayimila ake ndi achakwerawo!!!!!asiyeni chifukwa iwo si adyera koma koma akuyahula mmalo mwa chinamtindi cha anthu omwe akuvutika mmalawi muno

 23. The DPP are afraid of Chakwera. They want a weak opposition leader. Chakwera has a good background as pastor not like Peter who never worked in Malawi mtchona, he cant even speak his language Lomwe or Chichewa. The brother gave Peter the Presidence to protect him from cashgate, unfortunetly he died. Now who is going to protect Peter from cashgate of 577 billion? Chakwera will arrest you in 2019, the guilt are afraid.

 24. “We need not just the new driver but even the new bus altogether; one which is safe & sound,” quoting Mchere, one of the characters in Smouldering Charcoal MSCE English Literature. We dislike ur Personal Sydioncracies & unsound economic policies that ruin we the poor. We need new blood in the system; No more Recycled Politicians like urself boss (the top most); The George Chapondas; Patricia Kaliatis & so on & so forth……. Chakwera can probably be described as chosen by God to only redeem our loved Country Mother Malawi from fire, among others, thugs & corrupt idiots. U better step down honourably & accept ur failure b4 u r embarrassed in 2019 lyk de previous regime. Nothing to point in terms of devts since ur ascension into power in 2014 apart from Podium Castigations which u shower at those who oppose ur stupidity. Dr. Chakwera doesn’t even castigate u in de first place, he is just quiet koma inuyo mukungoteketseka nokha & u r busy kumutukwana why? Empty headed Chickens, after all an empty basket makes a lot of noise. Long live MCP, long live Dr. Chakwera 2019 Bomaaaaaa. God will vindicate Dr. Chakwera a true leader who doesn’t insult pple, a true man of God. Iweyo why don’t you go & continue teaching whether u were teaching in the Primary school or College & continue ur teaching or whatever u call lecturing career not Politics after all sudziwa kuyankhula komanso u don’t hv Leadership skills. Pumani voluntarily b4 we force u in 2019….

 25. Kkkkk akulephera peter & tava kuti project yakeyo yongobera dollar winiko watiuza munamutola kuti president wanuyo wa nyansi.Poti mai anu amavina mmisonkhano mukuona kuti zili bhoo

 26. This Idiot Why Dont He Go Back To Usa Where He Belong And Leave Our One And Only Last Hope President For 2019 Alone!!Come 2019 Enawa Akapume Ndiukalambawu.Dr Chakwera Boma Kale!!!!!

 27. Kodi ndimayesa Democracy itayamba ndi amipingo MAlawi?Kodi akamati pastoral letter amatanthauzanji?don,t put us in darkness as if we born yesterday we know the genesis of Malawi democracy.Stop insulting Chakwera if God chose him 2019 will tell for no one can block the finger of God.

 28. Dont talk stupid things against chakwera.He’s the only person who is expected with 99% of votes to win presidency seat in 2019 general elections.All democratic parties such as UDF DPP have failed to rule the nation properly.This is agood reason for mcp to come into the GTV.Iam talking abaut new mcp with new leader.

 29. If Chakwera has to leave politics and become a prophet,,,,,,,, then so should APM to go back to where he being (USA) and become SIR in lecturing rooms as he always does……

 30. Mungotaya nthawi yanu pachabe pangani zinthu zoti zikuthandizeni ndi mabanja anu.Musamalimbane ndi anthu oti analemera kale zakusogolo amadziwa ndi Mulungu yekha bs.2019 ndikutali and you dont know kuti mudzafikako ngakhale mukukamba zambiri apa.

 31. I can’t say he don’t know what he’s doing, yes he knows but we have to apologies to all Malawians for voting this useless man

 32. Amalawi ndayamba kukudabwani or president wanuyo akulimbana ndi chakwera wamtani??? Zikuonetserathu poyera kuti usogoleri wamkanika 2019 idakali kutali koma akumacita campaign, Pano m’malo mongoyendesa boma ngati president, kuti nchito zamanja ake zizamchitire umboni ndikusankidwanso mu term take yomaliza, ndi ntawi ya campaign iyi?? Akuoneserathu kuti simsogoleri othandiza antuameneyo Malawi ilibe msogoleri pakalipano kayatu odalira Ku boma ndimavuto kwambiri zafika poyipisisa nkalamba ampawi amasiye sangathandize, ameneyo. Munavotera muntu osaziwa cikhalidwe caciMalawi pepani zivutatu.

 33. Hahahahahahahahahahaha zoopsa u still love the person with one hand….people are dying UA busy talking shit bwt chakwera kodi DAVID sanali mfumu yet he was Man of God…mosses rule people…josephy he became a prime minister ndie chakwera watani za ntiii basi dziko lakukanikani inu….and UA president is sick…nokha simukuona apo with one hand mesa amati achila useless DPP rulling…l don’t knw kuti anthu mumaganiza bwanji…..mxiewwwwwwwwwwwww kupusa kutembeleledwa kupepera kapena chani…..mxiewwwww

 34. I wonder why Malawi is not moving foward. Instead of development they are busy compaigning. We are facing lot of problems that need solutions. And u are busy feeding pple empty endless promises to gain vote for 2019. So this means next 3yrs u wil be busy campaigning, not developments. Mulungu akukuonani.

 35. Kazichedwani ndi ndale,eni ake akumipanda akudyelera,inu masapota(kukanganilana maufumu) kumatukwanizana,kugawanika mitundu,njala ndiyo ilipoi,economy yavunda”””mukazaona nkuyu wayoyola masamba muzaziwe kt zinja layandikila” owelenga anawelenga,

 36. UDF-DPP 2019 BOMA…kapeni wayamba pamene nthawi ya kapeni sidafike,amene wati ziii sakulongolola,akuziwa kt even akangane iye adzalamula,naye lucius banda president wa udf ku parliament sakukhosomolapotu apa,coz akuziwa kt DPP ikati ili ndi mayi wake ndi bambo imati ndi UDF,pamene UDF ikati ili ndi kakhalamba kamake dzana,kodya minyewa kuleka fupa imat ndi MCP,so ziliko #2019.

 37. In portuquese language: Ese presidente nae impresta. Nao sabe xtas fazer. Esperar pastor Chakwera um dia comos shama de presidente republica de malawi. Nao falha nada. Musasewele naye chakwera wasanjikidwa dzanja lamulungu kuti adzatsogolere ana aIsalaeri mu ukapolo wa igupto.

 38. mmmh no wonder that isteed of unit & find soln to reasolve uncountable problems & develop our beauty country Mw economicaly,i think these dogs ar helples & wl not stop until 2019 wwoo!,nt thnking vg pple?

 39. Achitsilu a Petulo ndani ankadziwa kuti Bingu angalamulile dziko amapeza 1vote anthu mkumanena Nkhope ngati chosema sitikuchidziwa .koma Mulungu adatitulusa mukudulidwa ziwalo ndi UDF pomwe palibe ankakhulupilila kuti izachoka lero ilikuti Peter ndi DPP yake mukuona ngati ndiyamphamvu kuposa momwe idalili UDF? ambili mumanyoza MCP mwabadwa pompano Tiyeni tione limodzi ikatha 90 mins Ndine wa MCP koma DPP ya Bingu inandipangisapo .tsembwe koma siuyu mu Americano sakudziwa poyambila prayer wabwino amasungila tiyeni tizabweraso pompano 2019 Mwaneena zambili mwanyoza koma DPP yomwe timaidziwa siiyi lindani madzi apite Mwala okanidwa unaimika Kona Timamukana Bingu kunyoza anakonza dziko taimbila mmanja mu Americano munthu oti ku Malawi sadziwako uyu mavuto mbwe sakukondwa ndi ulamulilo wake Mulungu khulupililani

 40. Anthu inu kodi ndi angati andale omwe ndi am,busa? a Dumbo kodi sanali m,busa? nanga a mzomera Ngwira kodi si m,busa so so why always chakwera chakwera? Moyo wa munthu muli thupi ndi mzimu so lekani tirigu ndi nasongole zikulire limodzi kkkkkkk

 41. So when you are president you can dictate someone to change what he is doing & do as he pleases this is a foolish man does he have advisors?

 42. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 43. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 44. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 45. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 46. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 47. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 48. Mdima Kudana Ndikuunika, Posachedwapa Oipa Aonongeka Mulungu Amene A Chakwera Ndi A Malawi Akumupembeza Atilanditra Mmanja Mwaoipawo. Ngakhale Atapanda Kutelo Ife Sitizatumukira Oipayo. Ine Ndibanja Langa Tizadikira Utumiki Wa Chakwera Ndi Chiyembekezo Tioloka Yordan. Ambuye Dalitsani A Chakwera Pamodzi Ndi Mayi Malawi Kuti Oipayo A Chite Manyazi

 49. ndimulungu adamupititsa chakwera kundale ndicholinga choti apulumutse anthu adziko lake komaso mzika zakumalawi,pitala samadziwa chilichonse zaumphawi wa anthu akumudzi chifukwa kuno sikwawo pomwe chakwera wakulira kumudzi,anthu alibzy ukamba za chakwera sichifukwa china ayi kansalu koyera kamaoneka patali ndichifukwa chake anthu aukamba zachakwera koma choti adziwe ndichakuti akulimbana ndi mzimu woyera.

 50. DPP imango limbana ndi azinzawo basi-tamakambilanani za nzeru monga izi–vuto la madzi,vuto la magetsi tikudziwa mumangoti kush-gate zoona koma kodi simungapange zanzeru ndi kandalama kamapezekako kunena zoona sikuti ndinavapo kuti DPP anthu ake akambako chanzeru alomwe inu bwanji kodi thats why mumapita kumakataya nthawi ku mlakho kukaona mikanda yanchiwuno mwa azimayi so sad–dikilani nthawi ndi tsiku la kampeni not this tym..kodi poti ndinu opepera ndi chililime chodzadza nkamwacho nde basi opemphera alibe ufulu opanga ndale

 51. Awa achakwera palibe anachitapo vuto liri APA aona kuti kuchalichi atha kuwadyera anthu ndiye sizikuwakwana koma kukaba kuchipani anthu achinyengo awa ena izi mbamvazi popita ndikumati ndufuna kuthesa umphawi mmalawi muno koma palibe chimozi chikutika ndife tingolira mpaka lero

 52. Dont worry at the end uwill here our dear prist saying mr president umust resign coz he himself hav resign fro being apastor of malawi assembles of god

 53. Why not him leaving politics and continue being a judge or a lawyer? He should not pin point his colleague’s background job he has failed this nation and being a professor himself, he is running this nation as if he is herding cows

 54. I wonder most of the people who asseses chakwera, they dwell much on his decision of quiting religious things and joining politics. I think most people are being judgemental on his personality and NOT his capability to rule this country. Issue of faith is more personal, we don’t know Chakwera’s relationship with God,we don’t know what prompted him to make that choice. By the way what caliber of politiclans do we need in this country? If to lead people is ungodly or satanic or worldly we should stop praying for our leaders because they are agents of devil.

  1. Most of you just hate DPP, koma should hear about Jonah and stop basking in untruthfull kind of realities.Chakwera bolanso Tembo.

  2. My friend I second your writing . I think ignorance is misleading a lot of them. Politics according to me means ‘running government affairs in an honest manner’. Not Malawi’s concept of politics which means politicking mainly done by ungodly peoples like DPPs. NO NO NO

  3. Malawi it nid GOD otherwise mmmmmh I don’t know, Bible tells us that a nation without GOD direction it perish, see now everyone is crying let Almighty GOD help our leaders to sake God’s truth n Holiness people please.

  4. My God is watching.Vasiti paulendo Esther wa ku Palace wheather ulyk it or not.Dzanja lalemba pa khoma.Chakwera is the only hope for Malawi.If God says Chakwera who can say fweeeee!

  5. Proverb 29vs2 says when the righteous rule people rejoice but when the wicked rule people suffer . This is aclear indication that God wants righteous people to rule so that people can be happy. In malawi many people think politics is for the ungodly thats why they think men of God shouldnt join politics which is wrong. Should we say all those in politics are evil or what?

  6. Munthu Akaitanidwa Kukhala M’busa, Ameyenera Kukhala M’busa Mpaka Imfa. Zidakakhala Kut Sichoncho Bwezi Titawona David Kusiya Ufumu Kukhala Wa Nsembe Kapena Yesaya Kusiya Uneneri Kukhala Mfumu Kapena Eliya Kusiya Uneneri Kumulanda Dziko Ahabu Chifukwa Ahabunso Sankayendetsa Bwino Dziko. Kunena Zoona Zimene Adachta Chakwera Sizidachtikepo Mbiri Ya Bible. DPP Sikuyendetsa Bwino Dziko Tili Ngat Mmasiku A Ahabu. Koma Kut Atenge Dziko Chakwera Kuli Ngat Kut Kulamuliridwa Ndi M’dani Wa Mulungu, Mukuyembekeza Kut Dziko Lingafike Potani? Kod Simunawerenge Zimene Zidamchitikira Sauli? Iye Pokhala Mfumu Adalowerera Ntchto Ya Usembe Ndipo Mulungu Adakwiya Naye Namchotsa Pa Mpando Mkumuphera Ku Khondo. We Must Be Careful Wth The Calling. Chakwera Adagwa Mmanja Mwa Mulungu, Akufunika Kulapa Ndikubwerera Kwa Mulungu. Kulamuliridwa Ndi Iye Zinthu Zitha Kufika Poopsya.

  7. Don’t worry brother these people are used to crooked ways and think chakwera will change all these things completely. We need to accept that even the Christians can do better politics and refrain from castigations.

 55. Why dont peter mutharika himself return to his lecture job, where he is qualified to be. And if 3000 pple of mulanje voted chakwera just months after he joined politics, how many of them will him vote him 2019 after seeing how incempetent pter mutharika is, the person they voted in large numbers. As for charles mchacha no sane person wud be worried of whatever he says, Charles mchacha cannot even write his name in full without editting.

  1. Mchacha angosiya kunyoza anzake. He is nothing azingothokoza mulungu kuti kwaoko savotera munthu koma chipani. Madera ena uyu sangawine ump.

 56. Kkkkkkkk Inetu kudabwa Mmalo mopanga za madzi mwaambanso Campaign? mmmm koma kulawililatu kaya poti amati kugona pakati nkuambilila, koma osanyozana Sibwino ndinu Ma big nonse ndatukwana ngati?

 57. I come from mulanje, didn’t vote for Chakwera in 2014, but in 2019 I will give my vote to him! Chakwera.

 58. Kumalawi uphawi ndi mu mutumomwe anyani makamaka iwe othyoka mkono iwe siusataniki umenewo wasala mazi amozi iwe ull go soon ukuchedwa kukamba za mzako mmalo mo chita fighting wth hunger mkamwa movunda ndi mopanda manomo wamva khope yompindikayo

 59. Amene sumuopa sukhalanaye chidwi koma amene umamuopa ndiamene umamuwelenga .
  Moti pitala amuopa chakwela amene Uja ndi katundu 2019 boma

 60. Mr president simutha ndale ndipo mphatso zautsogoleli palibe, ndalama mudalandila frm Germany zilikuti kt mufufuze cashgate? nanga omwe adadyao alikut mukuononga dziko mulimbana ndi Chakwera why? y don’t u focus za mavuto omwe anthu akumananao Bwanji? mukadzaluza inu muli ndi kopita km amene mukudya nao, waku ndende basi.

 61. Akumuopa amenewo akudziwa kuti munthu yemwe akuwapatsa chiopsezo ndi chakera ndi chifukwa akumunena munya palibe kuvotera Dpp 2019 tidzavotera chakwera yemweyo olo mumunyoze motani

  1. Inu zaka 31yrs simunakhutisidwebe.Siyani nawo anzanu alamuleko kwasala zaka zingati kuti zikwane 31 pangani masamu nokha.Ngati mumakayika dikilani 2019 akuzawina kolapisa

 62. Achakwela kuwapatsa dziko nde lipondalamphawitu nanga munthu kusya za mulungu ndikukayamba za satana palinzelu?? Azawo amasya zoipa ndkuyambakupemphera iwowo akukasya kupemphela kukayamba zoipa,

  1. vuuuuuuuuuuuuuuuu bola kusiya mabuku kuyamba ndale ku church ndikumavayanso nangaaaa kusiya church ndikuyamba ndale ndiye pameneeepo olo o voter wo sangadabwe nazo mmmmmm

  2. Et or muliinu mungamuvotere munthu wachonchoyo? Pamenepopo mpofunikaso zitsiluzina zamaganizo ngat akewo nde zthakugwilizana

  3. Bambo ameneyu alibe nzeru ndithu. Nthawi yatha yoti YESU atenge ake, iwo ndi pamene akuthawa kulalikira mawu A MULUNGU. Mmmmmm akadakhala mwina akadasiya za ndale apite ku maitanidwe olalikira uthenga wa bwino.

 63. In Fact Ku Malawi Palbe Presdent Anachitapo Msonkhano Osatchula Dzina La Presdent Mzake Kunakakhala Ku School Ndnakat Ndzomwe Amawauza Aphunztsi Awo Bt Cc Nd Ndale Ma B Dats It

 64. In Fact Ku Malawi Palbe Presdent Anachitapo Msonkhano Osatchula Dzina La Presdent Mzake Kunakakhala Ku School Ndnakat Ndzomwe Amawauza Aphunztsi Awo Bt Cc Nd Ndale Ma B Dats It

 65. Joyce Banda pamisokhano yake amakamba zonyoza Peter, mapeto ake onyozedwayo anakhala president panoso chimodzimodzi ine ndikuona Chakwela 2019 akhala president wa dziko lino

 66. Zikuoneka kuti ziwanda zomwe zakhala zikuzunza dziko lino zayamba kuzindikira kuti kuunika kwayandikira. Men of God are better placed to lead God’s people.

  1. Waboza iwe boza lankunkhuniza muzalira 2019 landslide vicory.Inu kuunena kuti amwalire wafa wafa wafa.Mukuyesa kuti zingamusangalase mulungu alipo komanso ma ancsecitors akwawo amamenya nkhondotu.Mwalephera Bingu nkulu wake akumuyimiriranso kuti 2019 pavute patani azadutsa muzavomera.Muzanenanso kuti wabera chifukwa anasankha majudge alikwa Amerika amuwinasa mudzandivomera

 67. Nkhani ndi yakuti mumtengo wopanda zipatso anthu sagendamo. A DPP akuwonamo kanthu mwa DR Chakwera that’s why ali busy kugenda

  1. Tigendamo chiyani menemo mulibe kanthu akumuuza zowona kuti akapitilize za Ubusatu basi.What he is doing its just waste of tym.He cant defeat Muntharika u will believe me 2019 its only 29 month to go wait n see.

  1. Kuti kumeneko inu kwanu nkulira komweko dikilani nawo anzanu alamuleko zaka 31 za Kamuzu.Osati muzitiuza manyi anuwo onukha osatheka

 68. Iam siding the president because idont want MCP to rule this counry again and because of this guy(called chakwera) the party is loosing its value drastically.it is only jumbe who can restore the good image of this party so that people can now have trust in this party.chakwera is like jonah who deserted the work of God,he should go and continue the work of the lord.

  1. guys if you don’t know how best to express your anger and disatisfaction just remain silent because you like writting nosense.ihave seen some people who are contrary to my views but they do not critisise the way these guys do:rabson +kelvin.kutukwana for what?

 69. Pliz leave Chakwera osati mukasowa mfundo mtimisonkhano tanuto muzinyoza chakwera instead kukamba mfundo zavwino zoyendetsera boma lanuli yet you have a lot of problems which need to be solved in this country basi busy kumanena munthu. This shows that you don’t have gud idea on how you can rule the country am out

  1. Akapanda kukoza mavuto amene ali Kumalawi Azaluza Amalawi aseguka pano,,,paja mumaziwa kale kumpoto pitala sitimufuna tizaphatikizana ndi pa Central this is not Mornachy Gvnt,,,isaw big vission Dpp yikuzisiya 2019 briev me

 70. What Mutharika means is that Chakwera will loose in 2019 and will never be MCP candidate anymore therefore I can see Chakwera pozichosa manyazi muzamva akunena kuti ndaganiza zobwereranso ku za uzimu kkkkkkkkkkk

  1. U stand to be heartbroken come 2019. The moses u don’t like will triumph. The list of aspirants we have on the other side aren’t appealing.

  2. Koma apapa tisanamizanepo amene mudzakhale ndi mwayi ovota mudzaganize Bwino,,,, just imagine pano rate ili pa 1- 60 nde kudzafika chaka chovotera ifika 100,,, anthu akuvutika ni njala,,,,, bola kuyetsa mwayi chipani china,,,,

  3. kkkkk kod anthu mukuganiza kuti DPP izawina ? Analuza kamuzu Banda ndiye peter ndi ndani, ndale simuzidziwa mumufunse Sidick Mia waziwonera patali.

  4. Kongeresi singawine olo patavuta bwanji siyani kulota adeng’a inu fotseki, munthu lero ungamati kwacha kwacha usawi chani? kkkkkkkkkkkkkk

 71. Nanga iwe ukumukankhira mnzako iwe ubusao aiiiiiii kkkkkkk kukana ubusa kufuna mtendele wapansi apresdent athu ndioseketsa heavy .

 72. Doesnt dpp has a minister from ntcheu who is a pastor! This leader has never impressed me in whatever has spoken since his coming into presidency as he also came thru the back door by using the courts.

  1. Koma mumafuna muzimunena Chakwera azimunyoza azikhala pheee mwanamatu.2019 Pavute pasavute kuthidzimulanso molapisa muja mpaka 2024.Azamenyeranso kampeni afuna azatengeyo mpaka 2028 Chakwera kutsutsatu basi kwake

  2. frazer ngati padziko pano pali zitsiru,chitsiru chachikulu ndiiweyo,,,mavote ake okubawo?chili ndinzeru kodi chinkhalamba chanuchi?

 73. Inu mr chirwa mukufuna ife tikupatseni mareport achasowa ndi njaunju sizingatheke zimenezo kamasa tinapanga ife macadert kkkkkkkkk ndale zapamw ndizimenezo big.

 74. when you have empty headed president,an eccentric,those are the results. We are waiting of the results of Forensic report.Reports of Chasowa,Njaunju deaths

 75. ITS TRUE,LAZAROUS MUST GO BACK TO CHURCH,NDALE ZAMUPHUNZITSA KUTUKWANA KOMANSO UKALI.2019 AZALIRA CHOKWEZA M’DALA AMENEYI……

  1. Gyz ur happy ndiulamulilo wa DPP?Tiona ngat akumwela muzatigwesa,,ife tagwirizana no vote DPP,Kumpoto,,pakati Ochakwela,,kumpoto Mr Ibu ndi pakati ayi,,,,

 76. isaiah was a politician & a prophet, don’t think God do not know real politics games plus when you put God first other things second he’s gonna make you successful!#Think before you speak!!!!!!!!!”

  1. you are the one who is suppose to think b4 u speak….which Isaiah yu r talking about?musasochelese anthu mukristu ndindale palibe kugwilizana.Isaiah a book of prophecy not politics.

  1. Kumuopa kuti watani Chakwera wakoyo, iwe sukudziwa kuti anthu andale amayankhana. Akumunamizira zoti akakhale prophet, iwe monga sukudziwa kuti wanthawa nkhosa za mulungu ameneyu? Tangoganiza munthu kulimba mtima kusiya baibulo, kuyamba ndale ameneyu angazakumve kulira kwako iwe? Kunthawa m’manja mwa ambuye, kuteroku amaona kuchedwa ndi nkhani za ubusa eti?

  2. Pena mukut athawa Bible mwina kutheka Mulungu anaona ku Vutika kwa Malawi pa,,,njala,,komaso magazi apa 20july Nde Mulungu amutuma kut aliphure dziko Pamoto,,Koma am sure 70% anthu akulila ndi IBu,,osangalala ndi Mulakho wa lomwe 30%,,,,,God of Isriel whom ibriev bless Chakwera 2019,,,,we are tired with mornach GVt

 77. Thanks for capaigning for chakwera mwamutchukitsa kumeneko mupitirize because in 2019 his votes shall be 3000 times3000 musova,,, is it not in mulanje where a chaponda was1chased?

 78. Musalimbane ndi Chakwera inu a DPP, mukuona kuti wakusowetsani mtendere mpaka anthu 4 kutokota za a Chakwera pamsonkhano umodzi including president wadziko,munya muona imeneyo ndi MCP, tiyenawo Chakwera mbava zimenezo,MCP woyeeeee, Chakwera woyeeee, Sidik Mia woyeeeee, Richard Msowoya woyeeee, MCP 2019 ufune usafune Bomaaaaaaaaaaa!

Comments are closed.