Nyekhwe! Dzina labambo anga ayi – Paul Gadama waletsedwa
Pomwe kwangotsala maola ochepa kuti konveshoni ya chipani cha Democratic Progressive (DPP) iyambe, a Paul Gadama agwidwa njakata pomwe mwana wa malemu Aaron Gadama watenga chiletso chowaletsa kugwiritsa ntchito dzina la bambo awoli ponena kuti… ...