Ndidakuuzani lero ndi izi, wayankhula Usi pakusavana ku UTM
Mawu akulu akoma akagonera! Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi, wasambira m’manja akuluakulu a chipani cha United Transformation Movement (UTM) pachipwilikiti chomwe chabuka m'chipanichi ponena kuti iye adawachenjeza kale konveshoni isanachitike. Usi wayankhula… ...