Fodya akuphwanya ufulu wa a Malawi ochuluka
Ku Malawi munthu osasuta fodya kuyenda mtunda osachepera makilomita mazana asanu osapumako fungo la fodya ndichinthu chamtengo wapatali chofanana kuuzidwa ndi Yesu Mkhrisitu mwiniwake kuti machimo ako akhululukidwa ndipo uli mbali imodzi ya ufumu wa… ...