
Apha munthu chifukwa cha thelere
Apolisi m'boma la Mulanje akhazikitsa ntchito yosakasaka munthu yemwe akumuganizira kuti wapha mzake atamugwira akuba therere m'munda mwake. Mneneri wa apolisi m'bomali, Innocent Moses, wati izi zachitika usiku wa Lamulungu m'mudzi mwa Gojo kwa mfumu… ...