Talandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku – Kunkuyu
Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati boma lalandira mayankho opatsa chilimbikitso pa nkhani ya kafukufuku wa ngozi yomwe inakhudza wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi ena asanu ndi atatu. Poyankhura… ...