
Bambo wafa mgodi wa golide utadilizika ku Kasungu
Bambo wa zaka 45 wafa m'mudzi wa Maluzi ku Kasungu atakwililika mu mgodi omwe amakumbamo golide. Bamboyu dzina lake ndi Godfrey Chirombo. Malingana ndineneri wa polisi ya Kasungu, Sub-Inspector Jospeh Kachikho, a Chirombo pamodzi ndi… ...