MRA iyamba kugwiritsa ntchito tindege ting’ono ting’ono pothetsa ukamberembere ozembetsa katundu
Bungwe lotolera misonkho m’dziko muno la Malawi Revenue Authority (MRA) lati posachedwapa liyamba kugwiritsa ntchito tindege ting'ono ting'ono (drone) m’malire a dziko lino pofuna kuthana ndi anthu omwe amazembetsa katundu osiyanasiyana. M’modzi mwa akuluakulu a… ...