Mabuluku ong’ambang’amba avuta pa Malawi
Siumphawi koma kufuna kuyenda ndi nthawi kwapangisa achinyamata mu dziko la Malawi kugwa m’chikondi ndi mabuluku ong'ambang'amba. Mabulukuwa akumakonzedwa m’mawondo ndi mu ntchafu, kupangisa kuti khungu lizionekera kudzera m’mabowo munthu akavala. Kukula kwa mabowowa kukumasiyana.… ...