Aopa kusalandira malipiro, sitilaka yathetsedwa ku makhothi
Othandizira ogwira ntchito ku mabwalo ozengera milandu m’dziko muno athetsa kunyanyala ntchito komwe amapanga kuyambira mwezi watha. Izi zikudza patangotha tsiku limodzi pomwe boma la Malawi linaopseza kuti silipeleka malipiro a mwezi uno kwa onse… ...