![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2020/12/Lockdown-Partying-South-Africa-235x176.jpg)
Covid: aletsa mowa ku Joweni, odwala afika 1 miliyoni, a Malawi ochuluka akubwelelako
Nthenda yatisautsa mu chaka chino ya Covid yaluma mano ndi kupana mu dziko la South Africa kumene a Malawi ochuluka akubwelelako sabata ndi sabata. Malingana ndi malipoti ochokela mu dzikolo, anthu okwana 1 miliyoni tsopano… ...