
Amai a Sarah achezera odwala pa chipatala cha Kalemba
Gulu la amai la Sarah mu m'mpingo wa Living Waters International ku Bangula m'boma la Nsanje, lidakachezera odwala pa chipatala cha Kalemba mu nyengo yachikondwelero cha Khirisimisi. Malingana ndi mai Mbusa Priscilla M'bwana, chimodzi mwa… ...