
Anthu ena akufuna ine ndi a Chakwera tiyambane – Usi
A Michael Usi omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ati pali anthu ena amene akuyesetsa kuti iwo ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ayambane ndipo ati khalidwe lotelo limazunzitsa aMalawi, pamene… ...