Zilibe ndalama nyerere: miyezi yatha tsopano osalipila ma Kochi
Apambana ligi, kawiri konse kufika mu ndime yotsiliza ya mipikisano ndipo akukamba zopita ku mpikisano wa CAF koma manoma ali ndi mthumba moyela.Maluzi ngati khoswe wa mu kachisi. Malinga ndi malipoti, akatswiri a ligi chaka… ...