Boma lichotsa msonkho pa njinga zamoto
Boma la Malawi lalengeza kuti posachedwapa lichotsa msonkho omwe anthu amapeleka akagula ndikulowetsa mdziko muno njinga za moto kuchokera m'maiko akunja. Izi ndi malingana ndi nduna ya zachuma a Felix Mlusu omwe amayankhula kunyumba ya… ...