Siyani kuipitsira pa tchire, mangani zimbudzi, a Malawi alangizidwa
Anthu mdziko la Malawi auzidwa kuti asiye chizolowezi chomazithandizira pa tchire ndipo alangizidwa kuti ayambe kumanga komaso kugwiritsa ntchito zimbudzi zamakono moyenera. Izi ndimalingana ndi mkhala pa mpando wa khonsolo ya boma la Chikwawa khansala… ...