
Mithi wamangidwa kamba kofalitsa kuti MEC yafufuta maina a anthu ena mkaundula
Nthambi ya zachitetezo ya Malawi Police Service (MPS), yati Julius Mithi wamangidwa kamba kolemba pa tsamba lake la fesibuku kuti bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lafufuta anthu okwana 1,152,091 mundandanda wa anthu… ...