‘Thandizani osowa’ – Asilamu apemphedwa pa nyengo yokondwelera Eid Al Adha
Asilamu m'dziko muno awapempha kuti akhale othandiza osowa pomwe akusangala tsiku la Eid Al Adha lomwe amapha ziweto monga mbuzi, ng'ombe ndi nkhosa ndikupereka kwa anthu omwe ali osowa. M'modzi mwa akulu akulu a Bungwe… ...