
Khalani atcheru, zitetezeni ku namondwe otchedwa Jude
Pomwe namondwe otchedwa Jude wayandikira kulowa m'dziko muno kuchoka ku gombe la Nampula m'dziko la Mozambique, a Malawi amene tikukhala m'madera okhudzidwa maka mchigawo chakum'mwera, tiyeni tikhale osamala chifukwa pamapeto pa zonsezi, pali chiyembekezo kuti… ...