Lekani kuononga misonkho pomayenda m’misika, tsitsani mitengo ya zinthu – wadzudzura Mneneri David Mbewe
Mtsogoleri wa chipani cha Liberation for Economic Freedom (LEF) M'neneri David Mbewe, wauza wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi kuti asiye kuyendera misika ponena kuti akuononga misonkho yomwe itha kugwira ntchito zina zotukura… ...