O’Laza awa ndi panja penipeni – katswiri wa za malamulo
Inu mukuti ulendo uwu ndi wa ku Kenani, kambani ina chifukwa o'Chakwera alibe olo dontho la utsogoleri mwa iwo, ndendende zinachoka zija. Katswiri wa za malamulo, a Professor Danwood Chirwa athila ukali a Lazarus Chakwera… ...