CDEDI yati ana asabaidwe katemera wa Korona popanda chilolezo cha makolo
Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lachenjeza aphunzitsi onse komanso ogwira ntchito za umoyo kuti apewe kunyengelera ana asukulu kuti abayitse katemera wa Korona popanda chilolezo cha makolo. Bungweli lanena izi… ...