Wafika mkutho wachinayi wa Covid
...mapemphelo, ma bala, atha kuletsedwanso Ngati munakomedwa ndi msonkhano wa a ndale pachiwelu paja ndi kumayesa zipitilila, muganize kawili. Mliri wa Covid wamanga nthenje moti a boma akukumana kuti akhwimitse kachikena malamulo. Malinga ndi akatswiri… ...