![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2022/02/Southern-Bottlers-Malawi-235x176.png)
Khilisimisi ivutilapo chaka chino, fanta wakwera mtengo
Anthu omwe akuyembekeza kukhala ndi miyambo ngati ukwati ndi ina yomwe zakumwa zozizilitsa kukhosi zimafunika, alimbe mthumba chifukwa fanta, Coca-cola ndi azinzake akwera mtengo, ndipo nkhawa yagwira ana kuti mwina chaka chino khilisimisi itha kulepheleka… ...