Thupi la a Chilima lilowa m’manda Lolemba ku Nsipe
Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima akaika ku mudzi kwawo ku Nsipe m'boma la Ntcheu Lolemba sabata ya mawa. Poyankhura pa msonkhano wa… ...