DoDMA yati mabanja a ulesi sazilandira chimanga chaulere kuchokela ku Boma
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi m'dziko muno ya Department of Disasters Management Affairs (DoDMA) yati mabanja omwe ali ndikuthekera kogwira ntchito koma ndi a ulesi sazilandira thandizo la chimanga kuchokera ku Boma. Wanena izi… ...