
Flames yamaliza kuigwira ntchito Comoros
Timu yayikulu ya mpira wa miyendo ya Malawi 'The Flames' lero yakwapulanso Comoros ndi zigoli ziwiri kwa chete chete (2-0), mu mpikisano wa CAF African Nations Championship-CHAN pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe.… ...