Anthu okana kuti kuli Mulungu achita msonkhano, anyadila poti chiwelengelo chawo chikukula
Bungwe la anthu okana ndi okayika kuti kuli Mulungu kunja kuno, la Association of Secular Humanists (ASH), la ku Malawi kuno linachita msonkhano wawo wa pa chaka pachiwelu mu mzinda wa Lilongwe. Cholinga cha msonkhanowu… ...