Sizinafike poipa zinthu, zikadzafika ndizaimba nyimbo – watelo Lucius Banda
Mkulu uja anaimba nyimbo zodzudzula misonkho yochuluka, anaimbanso zodzudzula tsankho, ndi kudzudzulanso kukonda ma ulendo kwa adindo, lero ati zinthu ku Malawi kuno sizinafike poipa pofuna kudzudzula. Lucius Banda amene ndi mlangizi wa President Lazarus… ...