![Chiyanjano Mbeza](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/Chiyanjano-Mbeza-235x176.jpg)
Abale sakudziwabe komwe kuli Chiyanjano Mbeza
Patadutsa maola oposa 24 apolisi chimangileni mkozi wa nyimbo, Chiyanjano Mbeza pa mlandu omwe sukudziwika, achibale ake ati mpaka pano sakudziwabe polisi yomwe m'bale wawoyu akusungidwa. Mbeza yemwe amajambula nyimbo munzinda wa Blantyre, anamangidwa madzulo… ...