Watha vinyo mwa Pasuwa: nawo maule achapidwa ndi Siliva
A Nyerere atha kunamizila kuti anachapidwa koyenda, koma maule ndiye aswedwa pamaso pa akazi awo ndi apongozi awo. Pakwawo pompo awonetsedwa mbonaona. Ndi kutheka kuti ligi ija nawo sayionanso. Peter Mponda sanabwere kugawa ma suwiti.… ...