Sitikuona vuto pa kusankhidwa kwa mwana wa Chakwera – nyumba ya boma
Akuluakulu aku nyumba ya boma ati sakuona vuto lililonse pakusankhidwa kwa mwana wa mtsogoleri wa dziko lino Violet Chakwera Mwasinga kukhala mlembi ku office ya oyimilira dziko lino ku Brussels. Izi ndimalingana ndi oyankhulira mtsogoleri… ...